Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Atolankhani 57 Aphedwa Chaka Chino

$
0
0

Atolankhani 57 ati ndi omwe aphedwa chaka chino pa nthawi yomwe amagwira ntchito yawo.

Malinga ndi malipoti a News 24 atolankhaniwa 19 anaphedwa mdziko la Syria, khumi mdziko la Afghanstan, 9 mdziko la Mexico ndipo 5 mdziko la Iraq onsewa anali ali mmaiko a kwawo.

Chiwerengerochi ati ndi chotsika potengera ndi cha chaka chatha chomwe chinali  pa 67 kaamba koti atolankhani ambiri athawa mmaiko momwe muli zamtopola.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>