Anthu 5 Afa Kaamba ka Moto Mdziko la California
Anthu asanu ndi anayi afa ndipo pali chiyembekezo chakuti chiwerengero cha anthuwa chikhoza kukwera potsatira moto wamphamvu omwe unabuka mnyumba ina mdera la Oakland mu mzinda wa California. Malinga...
View ArticleSisteri Aphedwa Mdziko la Congo
Sisteri wina wa chipani cha Franciscan mdziko la Congo ati waphedwa mdera la Bakavu pa sukulu yomwe amagwirapo ntchito. Malinga ndi malipoti a wailesi ya Vatican anthu awiri omwe anatenga mipeni...
View ArticleAkhristu Afunitsa Kutsata Moyo wa Francis Chaviyere Woyera
Akhristu a pa tchalichi laFrancis Chaviyere Woyeraku NamweramuDayosiziya Mangochiati apitiriza kudzipereka pa ntchito yofalitsa uthenga wabwino monga momwe nkhoswe yawo inali kuchitira. Wapampando wa...
View ArticleAnthu 5 Afa pa Ngozi pa Msika wa Rudoviko M’boma la Ntcheu
Anthu asanu 5 afa ndipo ena ambiri avulala pa ngozi ya pa nsewu yomwe yachitika pa msika wa Rudoviko m’boma la Ntcheu. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Gift Matewere watsimikiza za...
View ArticleNjala Ikuyembekezeka Kuchepa M’boma la Chikwawa
Vuto la njala akuti likuyembekezeka kuchepa m’boma la Chikwawa potsatira ndondomeko yabwino ya ulimi wa nthilira imene yakhadzikitsidwa m’bomalo. Mkulu wowona za ndondomeko za chitukuko m’bomalo a...
View ArticlePapa Wapempha Atsogoleri Alimbikitse Ulamuliro Wabwino
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PAPA FRANCISCO wapempha atsogoleri a amayiko pa dziko lonse kuti alimbikitse ulamuliro wabwino pakati pa anthu omwe akuwatsogolera. Papa walankhula izi...
View ArticleKusamalira Anthu ndi Kusamalira Chilengedwe-Papa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wauza akuluakulu a mpingowu owona za utumiki kuti kusamalira anthu ndi njira imodzi yosamaliranso chilengedwe. Malinga ndi uthenga omwe...
View ArticleAmangidwa Kamba Kogwililira Msungwana wa Zaka 12
Apolisi m’boma la Dowa akusunga m’chitokosi bambo wina wa zaka 34 zakubadwa kwamba komuganizira kuti wagwilira mwana wa zaka 12m’bomalo. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant...
View ArticleOphunzira Achita Zionetsero Posakondwa ndi Kudula Mitengo
Ophunzira a sukulu ya pulaimale ya Nthumbi m’boma la Ntcheu anayenda ulendo wa ndawala posonyeza kusakondwa ndi kudula mitengo mwa chisawawa komwe kukuchitika m’madera ozungulira sukuluyo. Polankhula...
View ArticleKubwera Kwa Yesu Kudzetse Mtendere - Papa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Fransiscowapitiriza kupempha akhristu kuti kubadwa kwa Yesu Khristu kudzabweretse Chilungamo, mtendere komanso chimwemwe mmitima mwawo. Papa...
View ArticleBrother Henry Ibrahim a Chipani cha FIC Amwalira
Akulikulu la chipani cha ablazala mu mpingo wakatolika cha Brothers of Immaculate Conception of the Blessed Virgin Mary (FIC) ku Mzedi mu Arkdayosizi ya Blantyre alengeza za imfa ya Brother Henry...
View ArticleAphunzitsi Akukolezera Kuti Ana Aakazi Azisiyira Sukulu Panjira
Ophunziraa msukulu za pulaimale m’boma la Salima adandaula kaamba ka makhalidwe a aphunzitsi ena omwe ati akukolezera kuti ana aakazi azisiyira sukulu panjira. Ophunzirawa anena izi pa sukulu ya...
View ArticlePapa Apempha Akazembe Kuti Adzetse Mtendere
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akazembe a m’maiko kuti awonenetsetse kuti akudzetsa mtendere popewa za mtopola mu ulamuliro wao. Malinga ndi malipoti a wailesi...
View ArticlePapa Alimbikitsa Kufunika kwa Akhristu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisco wauza ansembe kuti akuyenera kutumikira anthu nthawi zonse osati kuti azikhala patsogolo kupanga mfundo zoyendetsera mpingo kaamba koti...
View ArticleMilandu ya Katengale ya Pulezidenti Zuma Iwunikidwenso
Bwalo lamilandu mdziko la South Africa lati ganizo lothetsa milandu 7 hundred 83 ya katangale ya pulezidenti wa dzikolo Jacob Zuma likuyenera kuwunikidwanso. Malipoti a wailesi ya BBC ati milanduyi...
View ArticleMutharika Wasintha Maudindo Ena
Mtsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wasintha ena mwa ma udindo a m’boma potsatira mphamvu zomwe ali nazo kuchokera mmalamulo oyendetsera dziko lino. Malinga ndi chikalata chomwe...
View ArticleAtolankhani 57 Aphedwa Chaka Chino
Atolankhani 57 ati ndi omwe aphedwa chaka chino pa nthawi yomwe amagwira ntchito yawo. Malinga ndi malipoti a News 24 atolankhaniwa 19 anaphedwa mdziko la Syria, khumi mdziko la Afghanstan, 9 mdziko la...
View ArticleAfa Atawombedwa ndi Chiphaliwali
Mamuna ndi mkazi wake ati afa chiphaliwali chitawaomba mmudzi mwa Chilinda kwa mfumu yaikulu Makanjira m’boma la Mangochi. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergent Amina Daudi wauza...
View ArticleAnthu M’boma la Mangochi Akuvutikira Fetereza wa Makoponi
Anthu okhala m’boma la Mangochi ati akukumana ndi mavuto kuti agule fetereza otsika mtengo wa makoponi chaka chino. Izi zadziwika pamene Mtolankhani wathu anafika ku malo ogulitsira feterezayu komwe...
View ArticleAna Awiri Akokoloka ndi Madzi a Mvula
Ana awiri akokoloka ndi madzi a mvula mu mtsinje wa Thang’ande m’boma la Neno. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant Raphael Kaliati wati anawa ndi Aufi Chiwembukomanso Benina Matemba onse a...
View Article