Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Bungwe la MEC latsutsa zoti likumayika zipangizo zosagwira bwino ntchito ku malo ena.

$
0
0

Bungwe lowona zachisankho la Malawi Electoral Commission MEC latsutsa malipoti oti likumayika zipangizo zosagwira bwino ntchito pa kalembera wa zisankho ku malo komwe anthu ena akuganiza kuti ndi komwe kuli ambiri otsatira chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive DPP.

Mukalembera wa zisankho mu gawo lachitatu yemwe watha posachedwapa, mphekezera zina zakhala zikumveka kuti mmadera ena bungweli limapititsa zida zosagwira bwino ntchito,zomwe anthu ena akhala akuganiza kuti zimachitika kuti anthu ena otsatira chipani cha DPP monga ku Phalombe asakhale ndi mwayi olembetsa mayina mkaundula wa zisankho za chaka cha mawa.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>