Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mtsogoleri Wa Chipani Cha Umodzi Ayamikira Boma

$
0
0

Chipani chotsutsa boma cha Umodzi chati sichikuonapo kulakwikwa kuli konse pa nkhani yoti alimi adzigulitsa chimanga chawo kwa Mavenda.

Mtsogoleri wachipanichi PROFESSOR JOHN CHISI ndi amene wanena izi pofotokozera RADIO MARIA MALAWI. Iwo ati, a Malawi akugulitsa chimanga chawo kwa mavenda  kaamba koti alibe njira ina yoti ndikupezera ndalama kaamba kakusowa kwa ntchito mdziko muno. PROFESSOR CHISI anati ma venda ndi anthu amene angathe kukhala ndi nthawi yabwino yosamalira chimanga ngati angagule chisanaumitsitse. Pamenepa  PROFESSOR CHISI anayamikira boma posafulumira kugula chimanga  kudzera mu misika ya ADMARC kaamba koti ndichosaumitsitsa zomwe ati chikhoza kukaonongeka. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>