Chiphwanya ndi Mlembi Watsopano wa CCJP
Aku likulu la mpingo wakatolika mdziko muno alengeza za kusankhidwa kwa a Martin Chiphwanya kukhala mlembi wa bungwe la chilungamo ndi mtendere m’dziko muno. A kulikulu la mpingo-wu ndi omwe alengeza...
View ArticleChaka cha Achinyamata pa Dziko Lonse 2019 Chidzachitikira Mdziko la Panama
Mpingo wakatolika m’dziko la Panama wati ndi wokondwa ndi uthenga umene walandira woti chaka cha achinyamata mu mpingowu pa dziko lonse chidzachitikire mdzikomo. M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa...
View ArticlePapa Fransico Aikiza Mmapemphero Akhristu Omwe Aphewdwa Mdziko La Egypt
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PAPA FRASISCO anaikiza mmapemphero akhristu a mpingo wina wachikhristuomwe avulazidwa komanso kuphedwa ndi a chiwembu mdziko la EGYPT. Akhristuwa...
View ArticleMtsogoleri Wa Chipani Cha Umodzi Ayamikira Boma
Chipani chotsutsa boma cha Umodzi chati sichikuonapo kulakwikwa kuli konse pa nkhani yoti alimi adzigulitsa chimanga chawo kwa Mavenda. Mtsogoleri wachipanichi PROFESSOR JOHN CHISI ndi amene wanena izi...
View ArticleNsomba Ya Shark Ivulaza Nsodzi Mdziko La Australi
Msodzi wina wavulala kwambiri mdziko la AUSTRALIA boti lomwe amapalasa mutalowa chi nsomba chotchedwa shark cholemera makilogram 200. Malinga ndi malipoti a BBC mwamunayu TERRY SELWOOD(SIWUDU) wa zaka...
View ArticleAbwenzi Amalitiri aku Uganda aku Malawi Apita ku Uganda
Abwenzi a AMALITIRI a ku UGANDA a kuno ku MALAWI motsogozedwa ndi episcope wa dayosizi ya mpingo wakatolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima ali nawo ku mwambowu. Akhristuwa adachoka mdziko muno pa 27...
View ArticleMwambo Wopereka Ma Degree ku ICI
Mwambo wopereka ma degree kwa ophunzira omwe amaliza maphunziro awo a Philosophy ku International Congregation Institute (ICI) m’boma la Balaka wachitika loweluka pa 3 June Chaka chino. Mmawu awo...
View ArticlePhalombe Catholic Parish has called upon well wishers to help in cons
The Parish Priest father Clifford Chiwanda made the call during a Fundraising paper Sunday that was held on Sunday 7th August 2016. The fundraising activity was aimed at sourcing funds to finish the...
View ArticleAwapempha Kuti Adzizipeleka Pokweza Ntchito Za Bungwe La Charismatic Renewal
Amsembe m’dziko muno awapempha kuti adzizipeleka pofalitsa mauthenga a ntchito zokweza bungwe la catholic charismatic renewal ndi cholinga choti lifalikire ponseponse mdziko muno. Bambo Bernard Tiyesi...
View ArticleA Mugabe Akuti Akufuna Kulandanso Minda Ina Ya Alimi A Chizungu
M’tsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha The Movement For Democratic Change a Morgan Tsvangirai m’dziko la Zimbabwewa dzuzula m’tsogoleri wa dzikolo president Robert Mugabe kaamba kamphekesera yoti...
View ArticleAkatekist A Ku Malawi Defense Force Apuma Pa Ntchito Yawo
Yemwe anali Katekist ku Malawi Defense Force a Benard Mukhula ku Zomba awayamikira kamba kodzipeleka pa ntchito yawo yotumikira mulungu kudzera mu mpingo wakatolika. Bambo Augustine Likado ndi omwe...
View ArticlePapa Francisco Wapempha Akhristu Kuti Azikhala Patsogolo Pakugwira Ntchito Za...
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PAPA FRANCISCO wapempha akhristu kuti azikhala patsogolo pakugwira ntchito za chifundo kwa anthu ovutika ndi osowa. Papa amalankhula izi pa mwambo wa...
View ArticleBungwe CWO Lilongwe Lipindula Ntchito Za Bungwe La TIVET
Bungwe La Technical Entrepreneur And Volcation Education And Training Authority (TIVET) lati lipitiliza kugwira ntchito zake ndi bungwe la amayi achikatolika mu arch-dayosizi ya Lilongwe. Mkulu wa...
View ArticleBungwe La MHRC Lalimbikitsa Ofesi Ya Social Welfare Kuti Isachite mantha...
Bungwe la Malawi Human Rights Commission lalangiza akuluakulu omwe amaona za ma ufulu a ana ku ofesi yoona za chisamaliro cha wanthu ya Social Welfare m’boma la Zomba kuti azigwira ntchito yawo mopanda...
View ArticleMbava Zoopsa Azigwira Mboma La Mchinji.
Apolisi m’boma la Mchinji agwira anthu atatu omwe akuwaganizira kuti ndi mbava zoopsa kwambiri zomwe zakhala zikubera anthu m’madera osiyanasiyana m’bomalo. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo...
View ArticlePapa ndi Okhudzidwa ndi Kusowa kwa Mtendere Mdziko la Syria
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransiskowati ndi wokhudzidwa ndi mavuto akusowa kwa mtendere omwe anthu a m’dziko la Syria akupitilira kukumana nawo. Papa wati magulu omwe...
View ArticleMpingo Wakatolika Ugwira Ntchito Zake Ndi Achinyamata
Msonkhano wowunikira momwe ntchito za achinyamata zikuyendera mu Dayosizi ya mpingo wakatolika ya Mangochi wachitika tsopano. Nthumwi zomwe zimakhudzidwa ndi nkhani zokhudza utumiki wa achinymatawu...
View ArticleAnthu okwana 43 Afa Pangozi Ya Basi
Anthu okwana 43 afa ndipo ena ambiri avulala pa ngozi ya basi yomwe anakwera itagubuduzika mdera la Nyamakete ku Hurungwe m’dziko la Zambia. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’dzikomo Charity...
View ArticleAmuna Awiri Amangidwa Ku Nsanje
Apolisi m’boma la Nsanje akusunga m’chitolokosi amuna awiri kaamba kowaganizira kuti anapha Njati mu nkhalango ya boma ya Mwamvi Game Reserve. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sargent Agnesi...
View ArticlePapa Wapepesa Dziko la Mexico, America
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wapereka uthenga wachipepeso kwa anthu omwe akhuzidwa ndi mphepo ya mphamvu yomwe yakhuza anthu a m’maiko a Mexico komanso America....
View Article