Quantcast
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Awalimbikitsa Kuti Akalembetse Mkaundula Wa Umzika

Anthu a m’boma la Zomba awalimbikitsa kuti asanyozere koma kuti akalembetse mayina awo mkaundula wa ziphatso za umzika.

Mkulu wa mu ofesi ya bwana mkumbwa pa nkhani za zakalembera a Tobias Lutepo ati kalembela-yu ndi wofuna kwambiri kamba koti azathandiza kuti anthu a m’bomalo akhaledi m’dzika zeni zeni za dziko lino.

Kalembera wa umzika mboma la Zomba akuti ayamba posachedwapa mbomalo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>