Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Chaka Cha Kubadwa Kwa Radio Maria Malawi Chidzachitika Pa 2 September 2017

$
0
0

Mwambo waukulu wokondwelera kubadwa kwa Radio Maria Malawi akuti udzachitika pa 2 september 2017 ndi mphwando la mayimbidwe (Radio Maria Malawi Choir Festival 2017) ku likulu la wailesi-yi ku Mangochi.

Malingana ndi malipoti a mu komiti yomwe ikuyendetsa dongosolo la mwambo-wu ati  mphwando la mayimbidwe  mu kwaya festival ya Radio Maria ya chaka chino , lidzakachitikira ku St Augastine Parish ku Mangochi Cathedral  pa 2 september 2017.

Padakalipano makwaya ochokera mmadayosizi osiyanasiyana mdziko muno alembetsa kale ndipo ati azafika ndi kudzatenga nawo mbari pa tsikuli. Radio Maria Malawi inabadwa pa 24 August 2017 ndipo kufikira pano yakwanitsa zak 18 ikufalitsa uthenga wachipulumutso pa dziko lonse. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>