Mfumu Ilimbikitsa Achinyamata Am’dera Lake Kuti Alimbikira Sukulu.
Achinyamata a m’dera la ku m’mwera cha kumadzuro kwa boma la Dowa awalimbikitsa kuti akhale olimbika pa nkhani za maphunziro. Senior Group Village Headman Kawiri ya mbomalo ndi amene yapeleka...
View ArticleAchinyamata Apempha Boma Kuti Liwathandize Ndi Ndalama Zoyambira Business.
Achinyamata m’dziko muno ayamikira boma kamba kokhadzikitsa ntchito zosiyanasiyana zomwe zayamba kuthandiza pa ntchito zokweza achinyamata m’dziko muno. Grace Scotch ndi amene wanena izi mwambo wa...
View ArticleAzipha pozimangilira mboma la Mangochi.
Bambo wina wa zaka 60 wa dzipha podzimangilira m’boma la Mangochi. Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo sergent Amina Tepani Daudi wati bambo-yu Umali Sabiti mutu wake...
View ArticleMpingo Wa Anglican Uyamikira Ubale Wake Ndi Mpingo Wakatolika.
Mpingo wa Anglican wayamikira m’gwilizano wa mphamvu umene ulipo pakati a mpingowu ndi mpingo wakatolika m’dziko muno. Mkulu wa mpingo-wu m’dziko muno Ambuye Brighton Vitta Malasa , omwenso ndi a...
View ArticleAsankhidwa Kukhala Mlangizi Wa Bungwe La YCW M’mayiko A Ku Mmawa Kwa Africa.
Akulukulu la bungwe la Young Christian Workers (YCW) mmayiko onse anasankha bambo Christopher Sichinga otumikira mu dayosizi ya Mangochi kukhala bambo mlangizi wa bungweli m’mayiko a mchigawo cha ku...
View ArticleAmayi 40 Apezeka Ndi Khansa Ya Khomo Lachiberekero Ku Mangochi.
Ofesi yoona za umoyo m’boma la Mangochi yapempha amayi kuti akayezetse khansa ya khomo la chiberekero ndi cholinga choti adziwe ngati ali ndi vutoli kapena ayi. Dotolo wa mkulu m’bomali Dr Henery...
View ArticleBungwe la MWW Aliyamikira Pothandiza Kuchepetsa Imfa Za Amayi Ndi Ana.
Boma kudzera mu unduna wa za umoyo lathokoza bungwe lolimbikitsa ntchito za uchembere wabwino la Maternity World Wide , kamba kodzipeleka pa ntchito zothandiza kuchepetsa imfa za amayi oyembekezera ndi...
View ArticleBambo Wina Wamwalira Pangozi Ya Pamsewu Mboma La Dowa
Bambo wina wa zaka 34 zakubadwa wafa atagundidwa ndi galimoto pomwe amafuna kuwoloka nsewu pa m’sika wa Chezi m’boma la la Dowa. Malingana ndi ofalitsa nkhani za a polisi m’bomalo Sergeant Richard...
View ArticleAwapempha Kuti Akonzekere Bwino Chaka Cha Nkhoswe Ya Dayosizi Yawo.
Episikopi wa mpingo wakatolika mu dayosizi ya mangochi ambuye montfort Stima apempha akhristu mu dayosiziyo kuti akonzekere bwino pa tsiku la chaka cha nkhoswe ya dayosizi-yi. Ambuye-wa alankhula izi...
View ArticleChaka Cha Kubadwa Kwa Radio Maria Malawi Chidzachitika Pa 2 September 2017
Mwambo waukulu wokondwelera kubadwa kwa Radio Maria Malawi akuti udzachitika pa 2 september 2017 ndi mphwando la mayimbidwe (Radio Maria Malawi Choir Festival 2017) ku likulu la wailesi-yi ku Mangochi....
View ArticleDC Wa Boma La Nsanje Wati Ayetsetsa Kutetedza Ndalama Zachitukuko.
Bwana mkubwa wa boma la nsanje a Gift Rappozo wati awonetsetsa kuti ndalama za mthumba la zachitukuko ku madera a aphungu m’bomalo (constituency fund) zikupinduliladi anthu okhala m’madera-wa pa nkhani...
View ArticleApolisi Alanda Galimoto Lomwe Akuliganizira Kuti Linachita Kubedwa
Apolisi m’boma la Machinga alanda galimoto ina ya mtundu wa Toyota Fortuner D4D , kamba koyiganizira kuti inachita kubedwa. Ofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha ku m’mawa kwa dziko lino Inspector...
View ArticleAchinyamata Awalimbikitsa Kuti akhale Akazembe A ntchito Zabwino
Achinyamata ampingo wakatolika awalimbikitsa kuti asafooke koma kuti akhale akazembe olimbikitsa ntchito ndi makhalidwe abwino pakati pawo. mmodzi mwa akuluakulu a bungwe lolimbikitsa moyo wa uzimu...
View ArticleBungwe La Mayi Khanda Likufuna Kufikira Amalawi Onse M’dziko Muno
Bungwe lolimbikitsa nkhani za uchembere wabwino la Mai Khanda Trust lati lili ndi mapulani ofuna kukuza ntchito zake m’dziko muno. Mkulu woona ntchito za m’bungwe-li a Edward Moses ndi amene wanena...
View ArticleMwambo wolonga mfumu ya Angoni a kwa Njolomole uchitika mwezi wa September 2017.
Zokonzekera mwambo wolonga mfumu ya angoni a kwa njolomole akuti zikuyenda bwino. Mwambo-wu udzachitika pa 21 September 2017 ku likulu la mfumuyi m’boma la Ntcheu. Wapampando wa komiti yomwe...
View ArticleAnthu a ku Salima Northwest Atsutsa Zoti Sakugwirizana ndi Phungu Wawo
Anthu otsatira chipani chotsutsa boma mdziko muno cha Malawi congress (MCP) ku mpoto cha kumadzulo kwa boma la Salima atsutsa zomwe zakhala zikumveka kuti anthu a mderali sakumufuna phungu wawo wa ku...
View ArticleZokonzekera Ulendo Wa Ku Malo Oyera Ku Rwanda Zikuyenda Bwino .
Komiti yomwe ikukonza ulendo wa ku malo oyera a Kibeho m’dziko la Rwanda komwenso kuli mbiri ya bungwe la Divine Mercy Apostolate yati padakalipano zonse zokonzera ulendowu zikuyenda bwino ....
View ArticleBungwe La ZAP Lipeleka Thandizo La Zipangizo Za Chipatala Ku ZOMBA.
Bungwe la Zomba Action Project (Zap) aliyamikira kamba kopeleka thandizo la zipangizo za umoyo ku chipatala chachikulu m’boma la Zomba cha Zomba Central. Wachiwiri kwa mkulu wa pa chipatala-chi mayi...
View ArticleMoto Wasakaza Nyumba 23 Za M’boma La Mangochi.
Moto wolusa wasaka nyumba 23 za anthu a m’mudzi mwa kafutula m’dera la mfumu yayikulu Nankhumba , m’boma la Mangochi. M’modzi mwa anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi-yi a Leonard Mbewe ati moto umene...
View ArticleAnthu ali ndi Udindo Woyezetsa Magazi
Anthu ati ali ndi udindo wokayezetsa magazi ndi cholinga choti adziwe momwe mthupi mwao mulili. M’modzi mwa dotolo wa pa chipatala cha Mwaiwathu Dr.Simon Chiumia anena izi mu mzinda wa Blantyre pa...
View Article