Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Zotsatira Za Mayeso A Junior Certificate Zatuluka.

$
0
0

Zotsatira za mayeso a Junior Certificate omwe ophunzira a form 2  analemba m’dziko muno  akuti zatuluka.

Bungwe la New Independent Academic Examination Council ndi lomwe linagwira ntchito yolembetsa mayeso-wa. 

Polankhula kwa atolankhani mu m’dzinda wa Blantyre mkulu wa bungwe-li mayi Phyles Kachingwe ati zotsatilazo zaonetsa kuti ophunzira ambiri omwe analemba nawo mayeso-wa sanachite bwino.

Iwo ati kuthetsedwa kwa mayeso-wa ndi boma ndi zina mwa zimene akuziganizira kuti ndi zomwe zakhala zikukolezelanso kusachita bwino kwa ana pa maphunziro awo. 


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>