Anthu Agwilitse Ntchito Bwino Zinthu Zomwe ali Nazo-ECM
Bungwe la ma episikopia mpingo wakatolika m’dziko muno la Episcopal Conference of Malawi (ECM) lati anthu m’dziko muno angachite bwino pa chitukuko cha miyoyo yawo ngati angachilimike pogwilitsa bwino...
View ArticleBambo Chingale Asankhidwa Kukhala A Vicar Genenal A Dayosizi Ya Mangochi.
Episikopi wa mpingo wakatolika mu dayosizi ya Mangochi olemekezeka Ambuye Montfort Stima wasankha bambo Frank Chingale kukhala Vicar General wa dayosizi-yi kuyambira pa 30 August 2017. Padakalipano...
View ArticleZotsatira Za Mayeso A Junior Certificate Zatuluka.
Zotsatira za mayeso a Junior Certificate omwe ophunzira a form 2 analemba m’dziko muno akuti zatuluka. Bungwe la New Independent Academic Examination Council ndi lomwe linagwira ntchito yolembetsa...
View ArticleMsonkhano wa bungwe la CWO Mu Dayosizi Ya Zomba
Msonkhano wa amayi a wakatolika mu dayosizi ya zomba wayamba pa 31 August 2017 ndipo udzatha pa 3 September 2017. Polankhula potsekulira msonkhano-wu Episikopi wa mpingo wakatolika mu dayosizi-yi...
View ArticleApempha Mabungwe Kuti Azigwira Ntchito Limodzi Polimbana Ndi Matenda A Edzi
Bungwe la National Aids Commission (NAC) lapempha mabungwe omwe siya a a boma omwe akugwira ntchito zolimbana ndi matenda a edzi m’boma la Zomba kuti azigwira ntchitozawo limodzi ndi a ku khonsolo,...
View ArticleAnthu 21 Afa Nyumba Itawagwera Mu M’dzinda Wa Mumbai M’dziko La India.
Anthu 21 afa nyumba ina yosanjikizana itawagwera mu m’dzinda wa mumbai m’dziko la India. Malingana ndi malipoti a BBC ambiri mwa anthu omwe afa pa ngozi-yi ndi omwe anali mkati mwa nyumbayi imene inali...
View ArticleMariatona wa Lokolo Atsekulidwa pa 15 October
Mwambo wotsekulira Mariatona wa lokolo akuti udzachitika loweruka pa 15 mwezi uno ku likulu kwa Radio Maria Malawi ku Mangochi. M’modzi mwa akulu akulu oyendetsa ntchito za Radio Maria Malawi a...
View ArticleAnsembe Sakuloledwa Kutsogolera Miyambo ya Maliro ya Anthu Odzipha
Mpingo wakatolika m’dziko la CANADA wati ansembe ampingowu sakuloledwa kutsogolera miyambo ya maliro aanthu amene amwalira mwakufuna kwawo. Ma-episikopi a mpingo-wu anena izi kudzera mu uthenga wawo....
View ArticleStation ya Sitima ya Nkaya Itha mu November
Gawo lachiwiri lomanga station ya sitima za pamtunda ya NKAYA m’boma la BALAKA akuti ikuyembekezeka kutha mwezi wa NOVEMBER chaka chino. Wofalitsa nkhani ku bungwe loona za sitima za pamtunda la...
View ArticleAmbuye Tamba Awonetsa Chidwi Chothandiza Radio Maria Malawi.
Episikopi wa mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba olemekezeka Ambuye George Desmond Tambala alimbikitsa ansembe mu dayosiziyo kuti apitirilize kuthandiza Radio Maria Malawi. Ambuye Tambala anena izi...
View ArticleAwapempha Kuti Asamaope Kukhala M’maudindo Osiyanasiyana
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awapempha kuti asamaope kukhala m’maudindo osiyanasiyana kamba koti kudzera m’maudindowa pomwe angathandize pa chitukuko cha dziko lino. Bambo Hennery...
View ArticleMariatona wa Lokolo Atsekulidwa pa 15 October
Mwambo wotsekulira Mariatona wa lokolo akuti udzachitika loweruka pa 15 mwezi uno ku likulu kwa Radio Maria Malawi ku Mangochi. M’modzi mwa akulu akulu oyendetsa ntchito za Radio Maria Malawi a...
View ArticleBambo Wina Amulamula Kukagwira Ukayidi Kwa Zaka 10 Pa Mulandu Wogwilira.
Bwalo loyamba lamilandu m’boma la Mwanza lalamula mwamuna wina wa zaka 28 zakubadwa kuti akakhale kundende kwa zaka 10 kaamba kopezeka olakwa pa mulandu wogwililira mwana wa msungwana wa zaka 15...
View ArticleAmangidwa Kamba Kopezeka Ndi Ndalama Zachinyengo.
Apolisi ku Lumbadzi m’boma la Dowa akusunga m’chitolokosi bambo wina wa zaka 22 zakubadwa kamba kopezeka ndi ndalama zachinyengo. Malingana ndi wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za polisi ku kanengo mu...
View ArticleBambo Willem Wester Amwalira
A Kulikulu la mpingo wakatolika m’dziko muno ku EPISCOPAL CONFERENCE OF MALAWI (ECM) alengeza za imfa ya bambo WILLEM WESTER omwe akhala akutumikira mpingowu ku ARCH DAYOSIZI ya Blantyre Bambo Wellem...
View ArticleAyamikira Anthu Chifukwa Chopereka Magazi
Bungwe lopereka magazi la MALAWI BLOOD TRANSFUNSION SERVICE (MBTS) layamikira anthu a m’boma la Ntcheu kaamba kodzipereka pantchito yopereka magazi pamene bungweli limagwira ntchito yotolera magazi...
View ArticleAkhiristu Apita Kumalo Oyera Ku Kibeho Mdziko La Rwanda
Akhristu amene ali pa ulendo wa ku malo oyeraa KIBEHO m’dziko la RWANDA awapemphaakuti asadere nkhawa pa zaulendowu kaamba koti zomwe achitazi ndi zopambana mu mbiri ya moyo wawo wa chikhristu. Izi...
View ArticlePapa Alimbikitsa Ubale wa Pakati pa Mpingo Wakatolika ndi Anglican
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu a mpingo wa katolika ndi Anglican kuti azigwilira ntchito limodzi ndi cholinga chofuna kulimbikitsa umodzi pakati pawo....
View ArticleAnthu Asanu ndi Ena Atatu Afa pa Ngozi ya Pansewu
Anthu asanu ndi ena atatu (8) afa ndipo ena avulala modetsa nkhawa mini-bus yomwe anakwera itagubuduzika ku Nguludim’boma la Chiladzulu. Malinga ndi m’modzi mwa omwe apulumuka pa ngoziyo mai Annie...
View ArticleApempha Akhristu Kudzipereka Pofalitsa Uthenga Wa Mulungu
Kudzipereka pa ntchito yakufalitsa uthenga wa Mulungu akuti ndi njira yokhayo imene imaonetsa chikhristu chenicheni. Abusa Joseph Maganga a mpingo wa CCAP kuchokera ku Chiradzulu ndi omwe anena izi...
View Article