Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Apempha Mabungwe Kuti Azigwira Ntchito Limodzi Polimbana Ndi Matenda A Edzi

$
0
0

Bungwe la National Aids Commission (NAC) lapempha mabungwe omwe siya a a boma omwe akugwira ntchito zolimbana ndi matenda a edzi m’boma la Zomba kuti azigwira ntchitozawo limodzi ndi a ku khonsolo, komanso a za chipatala m’bomalo.

Mkulu wa kuofesi ya bungwe-li m’chigawo cha ku m’mwera kwa dziko lino a Amidu Tung’ande ndi omwe anena izi pomwe amakumana ndi mabungwe-wa  komanso akulu-akulu oyang’anira ntchito za matenda-wa ndinso a zachipatala m’bomalo.

Iwo apempha adindo-wa kuti apange mapulani okhadzikika omwe athandize pa ntchito yolimbana ndi matendawa m’boma ndi mu m’dzinda wa Zomba.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>