Bungwe la COMPUTERS FOR MALAWI SCHOOLS lapeleka maComputer okwana (34) pa Sukulu ya Sekondale ya St Anthony ku THONDWE m’boma la Zomba.
Polandira katunduyu mkulu wazamaphunziro a Mc Gregory Alfandika omwe ndi EASTERN DISTRICT MANAGER ayamikira bungweli kaamba ka chidwi chawo chofuna kukweza maphunziro mdziko muno.