Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Awapempha Kuti Akhale Ndi Chidwi Chofalitsa Uthenga Wabwino Wa Mulungu.

$
0
0

Akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno awapempha kuti akhale ndi chidwi chofalitsa uthenga wabwino wa mulungu.

Mkulu wa mu ofesi yoona za mabungwe a utumiki wa apapa la Pontifical Mission Societies mu Dayosizi ya Mangochi Bambo Paul Rapozzo ndi omwe anena izi pa mnsokhano wa tsiku limodzi  wa otumikira ku Radio Maria Malawi ku Mangochi

A kulikulu la bungwe la utumiki wa apapa kuchokera la Pontifical Mission Societies ku likulu la mpingo wakatolika mdziko muno ku Episcopal Conference Of Malawi ECM ndi omwe anakonzera mavolontiyawa mbindikirowu ndi cholinga chowazindikilitsa zambiri zokhudza chibalalitso cha mpingo.

Mnsokhanowu unachitikira ku St John Guest House mu dayosizi ya Mangochi.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>