Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Ntchito Yakalembera Wa Umzika Ikupitilabe Mboma La Zomba

$
0
0

Ofesi yoona za kalembera m’boma la Zomba yati anthu amene sanalembetse mayina awo mkaundula wa ziphatso za umzika asadere nkhawa kamba koti ofesiyi ikupitilizabe kulemba anthu ku maofesi a bwana mkubwa wa bomalo.

Wachiwiri kwa mkulu wowona zakalembala-yu m’bomalo a mayi Mercy Satumba ndi omwe anena izi pofotokozera mtolankhani wathu. 

Iwo ati bomalo likufunitsitsa kuti ali yense alembetse ndi kukhala ndi chiphatso cha umzika.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>