Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

A Malawi 88 Omwe Anazembetsedwa Kuti Azipita Nawo M’dziko La South Africa...

Dziko la Mozambique lapulumutsa a Malawi 88 omwe likuwaganizira kuti anachita kuzembetsedwa ndi kuti azipita nawo m’dziko la South Africa. Ofalitsa nkhani za department yoona za anthu olowa ndi otuluka...

View Article


Mfumu Chikumbu Idana Ndi Zoti Atsikana Azithandizira Miyambo Ya Chikwati.

Mfumu yayikulu chikumbu ya m’boma la Mulanje yati sikugwilizana ndi m’chitidwe woti ana achitsikana azigwilitsidwa ntchito zovina pa miyambo ya zikwati kukhala ma (Dancing Queens). Mfumuyi yalankhula...

View Article


Apempha odwala Nthenda ya Khunyu kupita kuchipatala Mwansanga

Makolo m’dziko muno, awapempha kuti azifulumira kukaonana ndi madotolo , ngati awona kuti ana awo akusonyeza zizindikiro za matenda a kugwa. M’modzi mwa akulu-akulu ku bungwe lomwe limapeleka thandizo...

View Article

Apempha Boma kuti Lithandize ku Nkhanza zokhuzana ndi anthu a Khungu la...

Bungwe la Association Of Person  With Albinism in Malawi lati likhala lokondwa likamva kuti anthu amene akukhudzidwa ndi milandu ya kupha ndi kuzunza anthu akhungu lachi alubino m’dziko muno awazenga...

View Article

Ntchito Yakalembera Wa Umzika Ikupitilabe Mboma La Zomba

Ofesi yoona za kalembera m’boma la Zomba yati anthu amene sanalembetse mayina awo mkaundula wa ziphatso za umzika asadere nkhawa kamba koti ofesiyi ikupitilizabe kulemba anthu ku maofesi a bwana mkubwa...

View Article


Awayamikira Kamba Kodzipeleka Pa Ntchito Zotukula Parish Yawo.

Parish ya mpingo wakatolika ya Magomenero awayamikira kamba kodzipereka pa ntchito zotukula parishi-yo. Bambo mfumu a parishi-yi , bambo Ignatius Bokosi , ndi omwe anena izi pomwe amafotokozera...

View Article

Anamwino Adzipereka Pogwira Ntchito Zachifundo Pakati Pa Odwala Mdziko Muno

Anamwino m’dziko muno alonjeza kuti apitiliza ntchito yosamalira bwino odwala mzipatala zonse mdziko muno.   President wa gulu la anamwino kudzera pa tsamba la whatsap a blessings ganti , ndi amene...

View Article

Mpingo Wa Anglican Udzipereka Pa Ntchito Zokweza Achinyamata.

Dayosizi ya mpingo wa Anglican ya Uppershire yati ipitiliza kulimbikitsa ntchito za achinyamata mu mpingo-wu. Episikopi wa mpingo-wu mu dayosizi-yi , Ambuye Brighton Vitta Malasa , ndi omwe anena izi...

View Article


Akhazikitsa Komiti Pofuna Kupeza Gwero La Moto Womwe Unatentha Police...

Potsatira ngozi ya moto womwe wa sakaza katundu ndi nyumba yogona ophunzira pa Police Secondary School mu m’zinda wa Zomba, adindo okhudzidwa ndi nkhani-yi akhazikitsa komiti yofuna kupeza gwero la...

View Article


Mmodzi mwa Oyang’anira Chisankho Mdziko la Kenya Atula Pansi Udindo

Mmodzi mwa akuluakulu a bungwe loyendetsa chisankho mdziko la Kenya la Independent Electoral and Boundaries Commission (IEBC) watula pansi udindo wake patangotsala masiku ochepa kuti dzikolo lichititse...

View Article

Papa Wati Akhristu Kuyenera Kukahala Achikondi Ndi Olimba Pa Chikhulupiliro

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha akhristu kuti azikhala achikondi ndi olimba pa chikhulupiliro chawo. Papa walankhula izi pomwe amathililapo ndemanga pa...

View Article

Mmodzi mwa Oyang’anira Chisankho Mdziko la Kenya Atula Pansi Udindo

Mmodzi mwa akuluakulu a bungwe loyendetsa chisankho mdziko la Kenya la Independent Electoral and Boundaries Commission (IEBC) watula pansi udindo wake patangotsala masiku ochepa kuti dzikolo lichititse...

View Article

Apolisi Amanga Mzika 11 za Dziko la Ethiopia

Apolisi m’boma la Dowa amanga mzika za mdziko la Ethiopia khumi ndi m’modzi11 kaamba kolowa mdziko muno opanda chilolezo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’boma la Dowa, Sergeant Richard Kaponda wauza...

View Article


Anthu 73 Afa Mdziko la Mozambique

Anthu pafupifupi 73 akuti afa ndipo ena 160 avulula mdziko la Mozambique potsatira ngozi la galimoto la mtundu  Truck lomwe laphulika litanyamula mafuta. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC ngoziyi...

View Article

Chitukuko ndi cha Aliyense-Nankhumwa

Anthu m’dziko muno awapempha kuti achotse maganizo oti ntchito zachitukuko limayenera kugwira ndi boma.   Nduna ya za maboma ang’ono ndi chitukuko cha kumidzi olemekezeka a Kondwani Nankhumwa ndi omwe...

View Article


2000 Kwacha Yatsopano, Chisonyezo Cha Mavuto Azachuma

Kubwera kwa ndalama yatsopano ya 2000 kwacha yogwirana mdziko muno akuti ndi chisonyezo choti dziko la Malawi likukumana ndi mavuto azachuma adzaoneni. M’modzi mwa akatswiri pa nkhani zachuma mdziko...

View Article

Ayamikira Atolankhani Pa Nkhani Yofalitsa Mauthenga a Nkani Zokhuzana ndi...

Bungwe lomenyera ufulu wa atolankhani m’dziko muno la Media Institute Of Southern Africa (Misa-Malawi)  layamikira atolankhani momwe akugwilira ntchito zawo pofalitsa mauthenga okhudza mpheketsera...

View Article


Apempha Boma Kusintha Zina Mwandondomeko Zake Zoyendetsera Dziko.

chipani cholamula cha Democratic Progressive(DPP), kuti chikonze mavuto omwe anthu akukumana nawo m’dziko muno. Polankhula ndi Radio Maria Malawi mu m’dzinda wa Blantyre a Hamphrey’s Mvula ati chipani...

View Article

Galimoto Lapsa M’boma la Dowa

Galimoto la mtundu wa truck m’boma la Dowa ati lapsa potsatira ngozi yomwe galimotoli lachita pafupi ndi msika wa Chakhungu m’bomalo. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali SergeantRichard...

View Article

Apolisi Mchigawo cha ku M’mwawa Alonjeza Kupereka Chitetezo Chokwanira

Apolisi mchigawo cha kummawa kwa dziko lino ati akuchita chotheka kuwonetsetsa kuti anthu mchigawochi akulandira chitetezo chokwanira. Wofalitsa nkhani za apolisi mchigawochi Inspector Joseph...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>