Anthu pafupifupi 73 akuti afa ndipo ena 160 avulula mdziko la Mozambique potsatira ngozi la galimoto la mtundu Truck lomwe laphulika litanyamula mafuta.
Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC ngoziyi yachitika mdera lina chakumadzulo kwa mzinda Tete mdzikolo.
Malipoti ati anthu ena omwe avulalawa, amafuna kuba mafuta omwe tank ya galimotoli linanyamula.