Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Mpingo Wakatolika Utenga Mbali Polimbikitsa Ubereki Wabwino

$
0
0

Mpingo wakatolika m’dziko muno, wati upitiliza kudzipereka pa ntchito zolimbikitsa ntchito za ubereki wabwino pakati pa akhristu a mpingo-wu m’dziko muno.

Mkulu wa ku ofesi ya zofalitsa nkhani ndi mauthenga ku likulu la mpingo wakatolika mdziko muno, ku Episicopal Conference of Malawi(ECM)bambo Godino Phokoso,anena izi ku Mangochipomwe amakumana ndi nyumba zoulutsira mawu za mpingo-wu zaRadio Maria Malawi komansoLuntha Television.

Iwo apemphanyumbazi kuti zigwilizane ndi mpingowu pofalitsa mauthenga ozindikitsa akhristu a mpingo-wu kuti azitsatira njira za ubereki wabwino umene umalimbikitsa njira za kulera zachilengedwe.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>