Papa Apempha Anthu Alemekeze Ganizo la UN
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu kuti alemekeze ganizo la bungwe lowona za mgwirizano wa maiko a pa dziko lonse la United Nations lokhazikitsa mzinda wa...
View ArticleAdzudzula Trump Kamba ka Ganizo Loti Yerusalemu Akhale Likulu la Israel
Maiko ena pa dziko lapansi adzudzula mtsogoleri wa dziko la America, Donald Trump kaamba ka ganizo lake lopanga mzinda wa Yerusalemu kukhala likulu la dziko la Israel. Malipoti a wailesi ya BBC ati...
View ArticleAnthu Awiri Afa pa Ngozi ya pa Nsewu mu Mzinda wa Lilongwe
Anthu awiri afa pa ngozi ya pansewu yomwe yachitika pafupi ndi Area 25 Filling Station mu mzinda wa Lilongwe. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za a polisi pa polisi ya Kanengo mu mzindawo, Constable...
View ArticleAkagwira Jere Kamba Kogwililira Mwana Wake Wompeza
Bwalo loyamba la milandu mboma la zomba lalamula bambo wina wa zaka 35 zakubadwa kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka zisanu ndi zitatu (8) atamupeza olakwa pa mlandu...
View ArticleAnthu Atatu Afa pa Ngozi ku Mtengowanthenga-Dowa
Anthu atatu afa ndipo ena khumi ndi m’modzi (11) avulala pa ngozi ya pa nsewu yomwe yachitika pa Mtengowanthenga m’boma la Dowa. Wofalitsa nkhani za apolisi pa polisi ya Mponela m’bomalo, Sub Inspector...
View ArticleApolisi Mdziko la Turkey Amanga Anthu Omwe Akukhudzidwa ndi Chiwembu Cha...
Apolisi mdziko la Turkey ati amanga anthu angapo omwe akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi chiwembu chomwe chinaphetsa anthu 39 pa malo ena achisangalalo mdzikolo. Malipoti a wailesi ya BBCati anthu...
View ArticleApempha Makhansala Azibweretsa Zitukuko M’ma Ward Mwawo
Makhansala mdziko muno awapempha kuti azigwira ntchito yobweretsa chitukuko m’ma ward mwawo kuti anthu amene anawasankha aziwakhulupilira. Khansala wa ward ya Sadzi mu mzinda wa Zomba mayi Mercy...
View ArticleBwalo la Milandu Lilamula Anthu Asanu Kulipira 795,000 Kwacha
Bwalo lachiwiri la milandu m’boma la Machinga lalamula amuna asanu ndi m’modzi 6 kuti alipire chindapusa cha ndalama zokwana 795,000 kwacha kulephera apo akakhale ku ndende kwa zaka zitatu atapezeka...
View ArticlePapa ndi Wokhudzidwa ndi za Mtopola za Mdziko la Brazil
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndi okhudzidwa ndi zamtopola zomwe zachitika pa ndende ina zomwe zaphetsa anthu oposera makumi asanu 50 mdziko la Brazil. Papa...
View ArticleAnthu 170 Afa Mdziko La South Sudan
Anthu oposa 170 afa ndipo ena ambiri avulala pakumenyana kwa pakati pa mitundu iwiri ya anthu mdziko la South Sudan. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu oposa 200ndi omwe avulala pa kumenyanaku komwe...
View ArticleAmnesty Idzudzula Maiko a ku Ulaya
Bungwe lomenyera maufulu a wanthu pa dziko lonse la Amnesty Internationalladzudzula maiko a ku ulaya kaamba kozunza komanso kuchitira nkhanza anthu othawa kwawo a mdziko la Libya. Malinga ndi malipoti...
View ArticleApolisi Ayamikira Mgwirizano ndi Anthu a Kumudzi
Mkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mawa kwa dziko lino Commissioner Effie Kaitano wathokoza mafumu, anthu akumudzi komanso apolisi eni ake kaamba kogwirana manja pa ntchito yochepetsa umbava ndi...
View ArticleApempha Achinyamata Atenge Mbali Pothandiza Okalamba
Achinyamata a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti atengepo mbali pothandiza anthu okalamba komanso osowa mdziko muno. Wachiwiri kwa wapampando wa gulu la achinyamata a ku tchalitchi la St....
View ArticleObama Apempha Anthu Ateteze Ufulu Wa Democracy
Mtsogoleri wopuma wa dziko la America, Barrack Obama wapempha anthu m’dzikolo kuti akhale oteteza ufulu wa dimokalase. Malipotia wailesi yaBBCatiObamaamalankhula izi mu mzinda wa Chicago kudzera mu...
View ArticleANC Ikuyembekezeka Kusankha Mlowam’malo wa Zuma
Akuluakulu a chipani cholamula mdziko la South Africa cha African National Congress (ANC) akukonza zopeza mtsogoleri watsopano wa chipanichi yemwe atalowe m’malo mwa mtsogoleri wa dzikolo Jacob Zuma....
View ArticleApolisi Amanga Amuna Anayi pa Mlandu wa Kuba
Apolisi m’boma la Mangochi akusunga mchitikosi amuna anayi powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kubedwa kwa mu shop ina ya mzika ya dziko la Rwanda m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo...
View ArticleMpingo Wakatolika Utenga Mbali Polimbikitsa Ubereki Wabwino
Mpingo wakatolika m’dziko muno, wati upitiliza kudzipereka pa ntchito zolimbikitsa ntchito za ubereki wabwino pakati pa akhristu a mpingo-wu m’dziko muno. Mkulu wa ku ofesi ya zofalitsa nkhani ndi...
View ArticleAdindo Awayamikira Pothetsa Mphekesera za Opopa Magazi
Mafumu a m’boma la Zomba awayamikira kamba kogwirana manja ndi boma polimbana ndi nkhani zokhudza m’chitidwe wopopa magazi ndi nkhanza zomwe anthu a khungu la chi alubino akhala akukomana nazo...
View ArticleMadalaivala ali ndi Udindo pa Chitukuko cha Dziko
Anthu oyendetsa galimoto mdziko muno ati ali ndi udindo wopititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino. Wapampando wa bungwe la ma dalaivala mdziko muno la Drivers Association of Malawi, a John Harrison...
View ArticleMaphunziro a ku Simba Akupindula-PEA
Maphunziro a msukulu za masimba ati akuthandiza kuti ana azikhala otanganidwa ndi kuphunzira kuwerenga komanso kulemba. Mlangizi wa zamaphunziro mu zone ya St. Anthony Thondwe m’boma la Zomba, mayi...
View Article