Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Madalaivala ali ndi Udindo pa Chitukuko cha Dziko

$
0
0

Anthu oyendetsa galimoto mdziko muno ati ali ndi udindo wopititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino.

Wapampando wa bungwe la ma dalaivala mdziko muno la Drivers Association of Malawi, a John Harrison Banda anena izi ku Balaka pa mwambo wokhazikitsa bungweli m’bomalo.

Iwo ati madalaivala akuyenera agwire ntchito modzipereka kaamba koti kupanda iwo ntchito zambiri sizingayende bwino mdziko muno.

A Banda apempha madalaivala kuti agwirane manja pochepetsa ngozi za pansewu zomwe zikuchulukira mdziko muno.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>