Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Bambo Robert Masinda a Mdziko la DRC Apezeka Alibwino

$
0
0

Mpingo wakatolika m’dziko la Democratic Republic of Congo(DRC) wati ndi wokondwa ndi kumasulidwa kwa bambo Robert Masinda, ndi anthu ena asanu, omwe anagwidwa ndi gulu lina la zigawenga m’dzikomo.

Bambo Eliseo Tacchella, auza wailesi ya Vatican kuti bambo Masinda, akhala ali m’manja mwa zigawengazi kuchokera 22 January chaka chino pomwe zigawengazi zinawagwira limodzi ndi anthu ena asanu ogwira ntchito ku malo a Nino Baglieri mu mpingo-wu m’dzikomo.

Padakalipano mpingowu mdzikomo wati ndi wokondwa kuti bambo-wa apulumuka ndipo ali bwino.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>