Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Anthu 100 Afa Mdziko la Afghanstan

Anthu oposera 1 hundred afa mu mzinda wa Kabul mdziko la Afghanstan kaamba ka mabomba omwe anaphulitsidwa mu mzindawu. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu omwe achita chiwembuchi anayika mabombawa mu...

View Article


Bambo Robert Masinda a Mdziko la DRC Apezeka Alibwino

Mpingo wakatolika m’dziko la Democratic Republic of Congo(DRC) wati ndi wokondwa ndi kumasulidwa kwa bambo Robert Masinda, ndi anthu ena asanu, omwe anagwidwa ndi gulu lina la zigawenga m’dzikomo....

View Article


Papa ndi Okhudzidwa ndi Imfa ya Anthu 37 Mdziko la South Korea

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse, Papa Francisco wati ndi wokhudzidwa ndi imfa ya anthu omwe afa pangozi ya moto umene unabuka pa chipatala cha Sejong m’dziko la South Korea. Papa, wati...

View Article

PMS Iyamikira a Khristu Pothandiza pa Chaka cha Epifania

Ofesi yoona za mabungwe a utumuki wa a  papa ku likulu la mpingo wakatolika m’dziko muno ya Ponfitical Mission Societies(PMS) yayamikira chidwi chomwe akhristu a mpingowu anaonetsa pothandiza kuti...

View Article

Mpingo wa CCAP Upemphelera Mvula

Mpingo wa CCAP mu Sinodi ya Blantyre wachita mapemphero apadera, opempha mulungu, kuti adalitse dziko lino ndikulipatsa mvula yabwino. M’modzi mwa akulu-akulu mu mpingo-wu, m’busa Alex Maulana, wati...

View Article


Anthu 400 a Malawi Young Pioneer Alandirapo Zawo

Unduna wa zachuma mdziko muno ati walipira ndalama kwa anthu oposa400 omwe anali a Malawi Young Pioneer omwe anakhudzidwa ndi Operation Bwenzani. Mneneri mu undunawu a Davis Sado auza Radio Maria...

View Article

Papa Ayamikira Bungwe la Redcross Mdziko la Italy

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wauza bungwe lomwe limapereka thandizo kwa anthu omwe akumana ndi mavuto a njala,nkhondo, matenda ndi zina la Italian Red Cross kuti...

View Article

Arkidayosizi ya Blantyre Ipempha Akhristu Abwezeretse Chilengedwe

Arkidayosizi ya mpingo wa katolika ya Blantyre yalimbikitsa akhristu a mpingowu kuti abzale mitengo ngati njira imodzi yobwezeretsa chilengedwe mdziko muno. Vicar General wa arkidayosiziyi bambo...

View Article


Anthu Omwe Akuthandizidwa ndi CADECOM Akhale Odziyimira Pawokha-Ambuye Stima

Episkopi wa dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima apempha anthu omwe akuthandizika ndi bungwe lowoona za chitukuko mu mpingowu la CADECOMkuti akhale odziyimira pawokha...

View Article


Milandu Itatu Yogwilira ku Chikwawa Mwezi wa January

Apolisi m’boma la Chikwawa akusunga m’chitokosi bambo wina wa zaka 20za kubadwa yemwe dzina lake ndi William Masiyamphuka, kaamba komuganizira kuti wagwilira m’sungwana wa zaka zisanu. Padakalipano...

View Article

Makwaya Ayike Chikhristu Patsogolo

Makwaya a mu mpingo wakatolika ati akuyenera kuzindikira kuti akuyenera kuyika chikhristu  patsogolo pogwira ntchito zawo mu mpingo. Bambo Lawrence Kudzingo otumikira mu dayosizi ya Dedza ndi omwe...

View Article

Sister Apempha Papa Akambirane ndi Zigawenga za Al-Quaeda

Sisiteri wa m’dziko la Colombia yemwe akusungidwa mokakamiza ndi zigawenga za Al-Qaeda mdziko la Mali, wapempha mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco kuti athandize pa ntchito...

View Article

ECM Ilankhula pa za Nsalu Yodabwitsa pa Msika

Mpingo wa katolika mdziko muno wapempha akhristu ake kuti asagule nsalu yomwe ikupezeka pa msika yomwe ikusonyeza mayina a Papa Franciscko, Benedict 16. Mlembi wamkulu wa bungwe la ma episkopi a mpingo...

View Article


Apezeka Atafa Podzimangilira

Bambo wina wa zaka 37 zakubabdwa wapezeka atafa pozimangilira kwa Chikanda mu mzinda wa Zomba. Mneneri wa apolisi m’chigawo cha kummawa kwa dziko lino Inspector Joseph Sauka wauza Radio Maria Malawi...

View Article

Kabwerebwere Alamulidwa Zaka 9 ku Ndende

Bambo wina wa zaka 32 zakubadwa amulamula kuti akakhale ku ndende ndi kukagwira ntchito ya kalavulagaga kwa zaka zisanu kaamba kothyola shop ndi kuba katundu wa ndalama za nkhaninkhani. Wachiwiri kwa...

View Article


Papa Alimbikitsa Ubale wa Mpingo wa Katolika ndi Anglican

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco waonetsa chitsanzo cha ubale wabwino pakati pa mpingo wakatolika ndi wa Anglican. Papa wachita izi atakayendera akhristu a mpingo wa...

View Article

Bwanamkubwa Ayamikira Sukulu ya Ukachenjede ya DMI

Bwana-mkubwa wa boma la Mangochi a James Manyetera ayamikira sukulu ya ukachenjede ya DMI yomwe imayendetsedwa ndi amsembe a mpingo wakatolika mu chipani cha Missionaries of Mary Immaculate(MMI) kamba...

View Article


Khoti Lidzamvanso Mlandu wa a Chaponda pa 8 February

Bwalo la Chief Resident Magistrate m’boma la Zomba, likuyembekezeka pa 8 mwezi uno kuzapitirira kumva mlandu wa nduna ya kale ya zamalimidwe a George Chaponda omwe akuwazenga mlandu powaganizira kuti...

View Article

Apempha Akhristu Azipemphelera a Sisteri

Ophunzira a mpingo wa katolika msukulu za sekondale mdziko muno awapempha kuti akhale owonetsa makhalidwe abwino. Mkulu wa ku ofesi yoona za utumiki wa apapa ya Pontifical Missionary Societies (PMS) ku...

View Article

Mabungwe, MACRA Amemeza Anthu Akalembetse ma Sim Card

Mabungwe omwe si aboma ati akugwilizana ndi njira yoti aliyense akalembetse simu-kadi yake ya foni kamba koti zimenezi ndi zothandiza pa chitetedzo cha onse omwe amagwilira ntchito njirayi polumikizana...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>