Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Anthu 400 a Malawi Young Pioneer Alandirapo Zawo

$
0
0

Unduna wa zachuma mdziko muno ati walipira ndalama kwa anthu oposa400 omwe anali a Malawi Young Pioneer omwe anakhudzidwa ndi Operation Bwenzani.

Mneneri mu undunawu a Davis Sado auza Radio Maria Malawi kuti alandira mapepala ambiri a anthu omwe akufuna kulandira ndalamazi ndipo undunawu uli mkati mowunika mapepalawa kuti apeze anthu amene ali oyenelera kulandira nawo ndalamazi.

Iwo ati ntchitoyi ikupitilira ndipo akhala akusindikiza m’ma nyuzi pepala anthu omwe alandira ndalamazi kufikira onse oyenera, atalandira ndalama zawo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>