Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Bungwe la MEC Lakodzeka Kuchitisa Chisankho Mmadela Womwe Mulibe ma Nkhasala.

$
0
0

Bungwe lowona za Zisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission lati tsopano ndi lokonzeka kudzachititsa chisankho chachibwereza m`madela momwe mulibe makhansala m`dziko muno.

  Mmodzi mwa akuluakulu   a bugweli  Nancy Tembo  ananena izi ku Lilongwe pa mkumano wa atolankhani ochokera m`madera komwe chisankhochi chichitikire.

 Iwo anati bungwe lawo ligwira ntchito ndi atolankhani ndi cholinga choti uthenga wa chisankhochi ukafikire anthu mbiri ndiponso kutinso anthu wochuluka akaponye  vote.

Ponthililapo ndemanga pankhaniyi nkulu wa bungwe la Malawi Communication Reguratory Authority (MACRA) Fergus Lipenga anati bungwe lawo lipitiliza kugwila ntchito ndi bungwe lazachisankholi pa nkhani zonkhuza ulamulilo wa bwino komanso mamphuzilo aatolankhani.

Ma votiwa adzaponyewda pa 25 August ndipo boma lapeleka ndalama zokwana 40 millon zoti zigwilitsidwilen ntchito.

Malinga ndi bungwe ladzachisankholi,chisankho chidzachitika  ku Karonga,Chibanja ku Mzuzu, Msiksi ku Mangochi, Zomba Central ku Zomba ,komanso Luntcheza kunkhosolo ya Luntcheza ku Thyolo.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>