Anthu oposa makumi awiri akusowa nthaka itagumuka mdera la kumpoto chakumvuma mdziko la China.
Malipoti a BBC ati nyumba zankhaninkhani zomwe anthu ogwira ntchito pa kampani ina ya migodi mderalo amakhala zamila mmatope omwe adza kamba ka ngoziyi yomwe yachitika lachitatu mmawa.
Pakadali pano anthu khumi ndi anayi ndi omwe apulumutsidwa pangoziyi ndipo ntchito yofufuza anthu ena omwe akhudzidwa ati ikuvutirapo kamba ka mvula ya mphamvu yomwe yakhala ikugwa mderalo.
Anthu makumi anayi ndi omwe akudziwika kuti anali m’nyumba zawo panthawi ya ngoziyi.