Papa Francisco Apereka Mwayi woti Anthu Azawone Thupi la Malemu Padre Pio
Likulu lampingo wakatolika lalengeza kuti thupi la malemu Pio oyera yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Padre Pio adzalitulutsa mmanda kuti anthu adzakhale ndi mwai opereka ulemu kwa iye kuyambira...
View ArticleMwambo okondwelera kuti Ambuye Emanuel Kanyama ndi Ansembe awiri akwanitsa...
Mwambo okondwelera kuti Episkopi wa Dayosizi ya Dedza olemekezeka Ambuye Emmanuel Kanyama ndi ansembe ena awiri akwanitsa zaka 25 ali muunsembe uchitika Loweruka pa 8 ku parishi ya St Martin De-Poris...
View ArticlePapa Francisco Apempha Maiko Achitepo Kanthu Polimbana ndi Nkhaza.
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wabwerezanso kupempha maiko padziko lonse kuti achitepo kanthu polimbana ndi nkhanza zomwe akhiristu ndi magulu ena azipembedzo...
View ArticleDziko la Philippines Likhazikitsa Masiku a Tchuthi Pamene Papa Francisco...
Pamene mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco akuyembekezeka kukacheza mdziko la Philippines mwezi wa mawa, meya wa mzinda wa Manila mdzikolo walamula kuti anthu mu mzindawo...
View ArticleA Quest for a Better and Descent Malawi”
“A Quest for a Better and Descent Malawi” The Catholic Commission for Justice and Peace Media and Advocacy Statement on the Contemporary Socio-Economic and Political Context....
View ArticleAnthu omwe Ali ndi Zilema Zosiyanasiyana Ali ndi Mwayi wa Maphunziro a Luso
Unduna owona kuti pasamakhale kusiyana pakati pa akazi ndi amuna, ana ndi chisamaliro cha anthu olumala wapempha anthu omwe ali ndi abale omwe ali ndi zilema zosiyanasiyana kuti apite kumaofesi a...
View ArticleBwalo Lamilandu la ICC Siligwira Ntchito Mokondera
Mmodzi mwa akaswiri owona za malamulo komanso mkulu oweruza milandu mdziko muno wati samagwirizana ndi maganizo a anthu omwe amadzudzula bwalo la milandu la padziko lonse la International Criminal...
View ArticlePapa Francisco Wakhazikitsa Tsiku la 1 September Kukhala Lopemphelera...
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wakhazikitsa tsiku la pa 1 September chaka chino kuti likhale lopemphelera chisamaliro cha chilengedwe. Papa Francisco wakhazikitsa tsikuli...
View ArticleAnthu 22 Asowa Mdziko la China
Anthu oposa makumi awiri akusowa nthaka itagumuka mdera la kumpoto chakumvuma mdziko la China. Malipoti a BBC ati nyumba zankhaninkhani zomwe anthu ogwira ntchito pa kampani ina ya migodi mderalo...
View ArticleMabungwe Atenge Nawo Mbali pa Nkhani ya Magetsi
Kupereka mwayi ku mabungwe osiyanasiyana omwe siaboma kutenga nawo gawo pa ntchito zokhudza magetsi mdziko muno ati kungathandize kuti mitengo yamagetsiwa ikhale yotsikirapo. Wofalitsa nkhani ku...
View ArticleMfumu Zwelithini Ikuyembekezeka Kufika Mdziko la Zimbabwe
Mfumu yayikulu ya Angoni mdziko la South Africa Goodwill Zwelithini ikuyembekezeka kufika mdziko la Zimbabwe masiku akudzawa. Magulu osiyanasiyana omenyelera ufulu wa anthu mdziko la Zimbabwe ati mfumu...
View ArticleBambo Kamalo a mu Dayosizi ya Zomba Amwalira
Bambo Denis Kamalo omwe amatumikira mu dayosizi ya Zomba yampingo wakatolika amwalira. Malinga ndi mkulu wamuofesi yofalitsa nkhani za dayosiziyi Bambo Steven Likhutcha,Bambo Kamalo a mwalira...
View ArticleBungwe la UN Liwulura Mayiko Omwe Akuzunza Anthu
Bungwe la mgwirizano wa mayiko la United Nations UN lati liwulula mayiko omwe akulephera kupereka zilango kwa asilikali awo omwe akukhudzidwa ndi mchitidwe ozunza anthu osalakwa mmayiko omwe bungweli...
View ArticleBambo Kamalo Ayikidwa Mmanda
Mwambo oyika mmanda thupi la malemu Bambo Dennis Kamalo omwe amatumikira mudayosizi ya Zomba ngati wansembe mumpingo wakatolika wachitika lolemba ku Zomba Cathedral mu dayosiziyo. Bambo Kamalo amwalira...
View ArticleAnthu 40 Afa ndi Bwato
Anthu pafupifupi makumi anayi afa bwato lomwe anakwera litamira chifukwa chonyamula mopitilira muyeso mkatikati mwa nyanja ya Mediterranean mdziko la Libya. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu oposa...
View ArticleASisteri a Chipani cha Presentation Alimbikitsidwa mu Utumiki
M’bindikiro wa masiku asanu ndi atatu wa asisiteri a chipani cha Presentation for the Blessed Mary mu dayosizi ya Dedza watha lamulungu mudayosiziyo. M’bindikirowu omwe unachitika ndi mutu oti Mayi...
View ArticleMa episkopi Mdziko la America Adzudzula Apolisi
Maepisikopi a mdziko la America adzudzula apolisi ku mchitidwe omawopseza anthu oganiziridwa milandu omwe akuti wakula kwambiri mdzikolo. Ma episikopiwa adzudzula apolisiwo zitamveka kuti iwo...
View ArticleMakolo M’boma la Nsanje Apitiriza Kutsatira Myambo ina Yoyipa.
Makolo ena ku nsanje akupitirizabe kuchita miyambo ina yoipa monga kukwatiwitsa ana akadali achichepere komanso kuwagwiritsa ntchito zokhwima zomwe ati zikumakolezera ana ambiri kusiya sukulu. Mkulu...
View ArticleHostel ya Atsikana Imangidwa pa Secondary ya Liwonde M’boma la Machinga.
Kumangidwa kwa hostel ya atsikana pa sukulu ya Secondary ya Liwonde m’boma la Machinga kuthandiza kuti atsikana ambiri ayambe kuchita bwino pa maphunziro awo. Mphunzitsi wa mkulu pa sukuluyi a Welson...
View ArticlePulezidenti Kiir Wakana Kusayinira Mgwirizano Wodzetsa Mtendere
Mtsogoleri wa dziko la South Sudan Salva Kiir wakana kusayinira mgwirizano odzetsa mtendere pakati pa iye ndi magulu owukira boma mdzikolo. Pulezidenti Kiir wakana kusayinira panganoli posachedwapa...
View Article