Quantcast
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Chipani cha Mofolo Chidzoza a Blazala Awiri Kukhala Madikoni

A Blazala awiri a chipani cha Mofolo woyera loweruka awadzodza kukhala madikoni mu mpingo wakatolika .

Mwambowu omwe unachitikira ku parish ya St Louis  Montfort ku Balaka  anatsogolera ndi episkopi wa dayosiziyi ambuye Montfort Sitima.

Mu ulaliko wawo Ambuye Sitima anati Mulungu amayitana anthu ake kuti akagwire ntchito yolalikira mthenga wachipulumutso ponse ponse.

Polankhulanso utangotha mwambowu madikoniwa ati ndi okondwa kuti Mulungu wawathandiza kufikira pano pomwe adzozedwa kukhala madikoni ndipo ati adzipereka pa ntchito zotumikira mulungu kudzera mu mpingowu.

Madikoni omwe adzozedwawa ndi a Anthony Chilolo ndi Peter Makina.

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>