Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Anthu Asanu Afa ndi Bomba Mdziko la SomaliaAnthu Asanu Afa ndi Bomba Mdziko la Somalia

$
0
0

Anthu asanu afa ndipo ena asanu ndi awiri avulala kamba ka bomba lomwe linaphulitsidwa pa malo ena odyera mu mzinda wa Mogadishu mdziko la Somalia.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC munthu yemwe wachita izi ati anayimitsa galimoto lake panja pa malowo momwe munali bomba lomwe linaphulitsidwalo.

Malipoti ati gulu la zigawenga za chisilamu za Al-Shabab lavomera kuti ndi lomwe lachita chiwembuchi.

Gululi lomwe lili pansi pa gulu la zigawenga za Al-Qaeda lakhala likuchita za uchifwamba mdziko la Somalia kuyambira mu chaka cha 2011.

Trending Articles

Mdima unadetsa dziko

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>