Anthu Asanu Afa ndi Bomba Mdziko la SomaliaAnthu Asanu Afa ndi Bomba Mdziko...
Anthu asanu afa ndipo ena asanu ndi awiri avulala kamba ka bomba lomwe linaphulitsidwa pa malo ena odyera mu mzinda wa Mogadishu mdziko la Somalia. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC munthu yemwe...
View ArticleAmbuye Musikuwa ati Achinyamata Akhale a Makhalidwe AbwinoAmbuye Musikuwa ati...
Episkopi wa mpingo wakatolika wa dayosizi ya Chikwawa, Ambuye Peter Musikuwa walangiza ophunzira msukulu zosiyanasiyana za ukachenjede m’dziko muno kuti asalore kuti ena aziwapotoza ndi kuti azitsatira...
View ArticlePapa wati Akhristu Amuyike Mmapemphero
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti amuyikize mmapemphero pomwe akukonzekera ulendo wake wokayendera anthu othawa kwao pa doko la Lesbos mdziko la...
View ArticleChiwerengero cha Akhristu Akatolika Chakwera
Lipoti latsopano lomwe likulu la mpingo wakatolika latulutsa, lasonyeza kuti chiwerengero cha akhristu a mpingowu chakwera kwambiri mu zaka zisanu ndi zitatu zapitazi. Lipotilo lati kuyambira mchaka...
View ArticleMkulu wa Maepiskopi Mdziko la Greece wati Ali ndi ManthaMkulu wa Maepiskopi...
Pamene mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ndi atsogoleri a mpingo wa Orthodox akuyembekezeka kukayendera anthu othawa kwao pa chilumba la Lesbos mdziko la Greece, mkulu wa ma...
View ArticleNjala Ikubwezeretsa Ntchito Za Chitukuko
Mavuto anjala ati akubwezeretsa m’mbuyo ntchito za chitukuko komanso maphunziro ku dera la kum’mwera kwa boma la Neno. Phungu wa derali Mayi Mary Maulidi ndi omwe anena izi pomwe bungwe lina lomwe sila...
View ArticleBungwe la Amayi Lilonjeza Kutukula Dayosizi
Wapampando watsopano wa bungwe la amayi mu mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba , Mayi Elizabeth Meke wati komiti yawo ipitiliza kudzipeleka pa ntchito zotukula dayosiziyo. Mayi Mekeanena izi...
View ArticleMpingo wa Anglican Ukulimbikitsa Maphunziro a Atsikana
Mpingo wa Anglican mu dayosizi ya Uppershire kudzera mu project yomwe mpingowu unakhadzikitsa ya Msamama Community Intergrated wati upitiliza kudzipeleka polimbikitsa maphunziro atsikana. Mkulu...
View ArticleAmbuye Stima Ayamikira Asisteri a DMI Pa Chitukuko
Episkopi wa dayosizi ya Mangochi olemekezeka Ambuye Montfort Stima ayamikira asisteri achipani cha Daughters of Mary Immaculate (DMI)kamba kolimbikitsa zitukuko zosiyanasiyana mu dayosiziyo. Ambuye...
View ArticleMpingo Upempha Boma la Nigeria Likambirane ndi Gulu la Boko Haram
Mpingo wakatolika mdziko la Nigeria wati boma la dzikolo likuyenera kuchita zokambirana ndi zigawenga za gulu la Boko Haram ndi cholinga chofuna kupulumutsa atsikana 2 hundred a mtauni ya Chibok omwe...
View ArticleChivomerezi Chapha Anthu Asanu ndi Anayi Ku Japan
Anthu pafupifupi asanu ndi anayi afa ndipo ena avulala m’dziko la Japan kaamba ka chivomerezi chomwe chagwedeza mthaka ya dzikolo. Malingana ndi malipoti a wailesi ya BBC anthu ochuluka anathawa...
View ArticleArkidayosizi ya Blanytye Iyamikira Bungwe la CFM
Arkidayosizi ya Blantyre mu mpingo wa Katolika yayamikila mgwilizano ndi luntha lomwe bungwe la mabanja a chi khristu la Christian Family Movement (CFM) ku parishi ya St Pius likuonetsa potenga mbali...
View ArticleMpingo Wa Katolika Uchita Chaka Cha UtumikiMpingo Wa Katolika Uchita Chaka...
Episkopi wa dayosizi ya Dedza ambuye EmmanuelKanyamawapempha achinyamata kuti akhale ndi udindo waukulu podzipeleka pa ntchito zotumikira mpingo kudzera mmautumiki osiyanasiyana. Ambuye Kanyama anena...
View ArticleMaphunziro a Pafupipafupi ndi Othanza kwa Achinyamata
Parishi ya Lirangwe mu Arkidayosizi ya Blantyre ya mpingo wa katolika yati ntchito yosintha kaganizidwe ka achinyamata ati ingatheke ngati pangakhale maphunziro a pafupipafupi kwa achinyamatawa. Bambo...
View ArticleAnthu Othawa Kwao Afa Bwato lomwe Anakwera Litamira mu Nyanja ya Mediterranean
Anthu othawa kwawo mazanamazana ati amira bwato lomwe anakwera litamira panyanja yaikulu ya Meditereanneanm`dziko la Egypt. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, anthu 41 ndi omwe apulumitsidwa pa...
View ArticlePapa Francisco Achita Zokambirana ndi Presidenti wa Dziko la Central African...
Mtsogoleri wa dziko laCentral African Republic, a Faustin Archangel Touadera ali ku likulu la mpingo wakatolika ku Vatican komwe akuchita zokambirana ndi mtsogoleri wa mpingo wa katolika Papa...
View ArticleAlimi Azigwiritsa Ntchito Zipatala Za Mbewu
Alimi m`boma la Mulanje awapempha kuti azigwiritsa ntchito zipatala za mbewu zomwe ofesi ya za malimidwe inakhazikitsa m`bomalo ngati njira yothanirana ndi matenda osiyanasiyana omwe amagwira mbewu....
View ArticleMfumu Zwelithini ya Mdziko la South Africa Ikuyembekezeka Kudzudzula Anthu...
Mfumu yachizulu Good-will Zwelithini ya mdziko la South Africa ikuyembekezeka kulankhulapo popempha mzika za dzikolo kuti zisiye kuchitira mtopola mzika za mmayiko ena zomwe zikukhala mdzikolo pa...
View ArticleSister Fortina Saiwa Atisiya
Aku likulu la chipani cha asisiteri cha Tereza Woyera mu Arkdayosizi ya Lilongwe alengeza za imfa ya Sister Fortina Saiwa. Iwo amwalira lachiwiri ku chipatala cha Mlale m’boma la Lilongwe. Sister...
View ArticleUnduna Upempha Anthu Asamukire Kumadera Okwera
Unduna woona za ulimi wa mthirira ndi chitukuko cha madzi wapempha anthu omwe akukhala m`madera otsika m`boma la Karonga kuti asamukire kumadera okwera. Unduna wu wanena izi kudzera m`chikalata...
View Article