Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Machar Alumbilitsidwa Kukhala Wachiwiri kwa Pulezidenti

$
0
0

Mkulu wa gulu lowukira boma m’dziko la South Sudan Riek Machar amulumbiritsa kukhala wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dzikolo ndi cholinga chofuna kukometsa pangano lodzetsa mtendere ndi m’tsogoleri wa dzikolo Salva Kiir.

Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC a Machar abwelera mdzikolo kuchokera mu mzinda wa Juba posachedwapa, kamba ka boma la mgwirizano lomwe lakhazikitsidwa ngati njira yothetsera kusamvana komwe kunalipo kwa zaka ziwiri.

Malipoti ati anthu 10 sauzande anaphedwa ndipo ena osachepera 2 miliyoni akusowa pokhala kamba ka nkhondo yomwe yakhala ikuchitika mdzikolo. 

A Machar anathawira mu mzinda wa Juba m’mwezi wa December m’chaka cha 2013 itangoyambika nkhondo yapachiweniweniyi.

Trending Articles

Mdima unadetsa dziko

<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>