Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

ECM Lapereka ndalama ku Bungwe la MISA Malawi

$
0
0
Likulu la mpingo wa katolika dziko muno ECM,kudzera ku nthambi yake ya zachitukuko ya Social Development Directorate lapereka ndalama zokwana 5 hundred thousand kwacha ku bungwe la atolankhani la MISA Malawi kuti zithandizire zokonzekera tsiku lokumbukira ufulu wofalitsa nkhani.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875