Mwambo wotsekulira Radio Maria Mariatona 2016 uchitika mawa ku Parish ya St.Louis Montfort ku Balaka mu dayosizi ya Mangochi,pali chikonzero choti akatsogolere misa yotsekulira Mariatona ndi ambuye Montfort Sitima adayosizi ya Mangochi ndipo zonse zikayamba ndi m'bindikiro nthawi ya 8 koloko mmawa .
↧