Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Anthu Khumi Afa pa Ngozi ya Bus

$
0
0

Anthu khumi afa ndipo ena 62 avulala bus yomwe anakwera itachita ngozi mdera la Songo mdziko la Mozambique.

Malinga ndi malipoti bus-yo yomwe ndi ya Kampani ya Nyamende nambala yake KMZ 56 ZN imachokera mdziko la South Africa kupita mu mzinda wa Blantyre ndipo inanyamula mzika za mdziko la Malawi.

Akuluakulu a basiyo ati padakali pano anthu omwe avulalawo agonekedwa ku chipatala chachikulu cha Mwanza.


Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>