Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

UMOYO PATSOGOLO

$
0
0
Sabata yathunthu yoganizira zaumoyo,yayamba lero mdziko muno pamene zipatala zalimbikitsa ntchito yopereka katemera wa Ana ndi zithandizo zina kwa ana osaposera zaka zisanu.
Pothilirapo ndemanga zasabatayi, ofalitsa nkhani zaumoyo pachipatala cha Mangochi a Anold Ndalira,ati sabatayi ikhala yofunikira kwambiri pomwenso ana,amai oyamwitsa ndi oyembekezera akhale akuwunikiridwa za thanzi lawo,zomwe zichititse kuti ayikidwe mundondomeko zapadera akapezeka ndi vuto lonyentchera.A Ndalira ati zinanso zomwe chipatalachi chichite msabatayi ndikupereka mankhwala a njoka za mmimba ndi katemera wa Vitamin, yemwe amathandiza kuchepetsa vuto la matenda a maso.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 1875

Trending Articles


Mdima unadetsa dziko



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>