Ndewu Pakati Pa Njoka ndi Chule
Ulaliki titled Ndewu Pakati Pa Njoka ndi Chule by Father James Chizuma
View ArticleNZIKA ZILI NDI UDINDO PA ZISANKHO ZA 2014-MEC
Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC), lati nzika za m’dziko lino zikuyenera kuonetsa udindo wawo potenga mbali pazisankho zachaka cha mawa polembetsa m’nkaundula wa mavoti. Wapampando wa bugweli...
View ArticleNYUMBA YA MALAMULO IVOMEREZA BOMA KUTENGA NGONGOLE YA 14.8 BILLION KWACHA
Nyumba ya malamulo mdziko lino yavomereza Boma kutenga ngongole ya ndalama zokwanira 14.8 billion kwacha zoti ligwiritsire ntchito yomangira msewu wa Mzuzu- Nkhatabay. Nduna ya za chuma Olemekezeka a...
View ArticleA MANG'ANJA AKUMANA- CHILUKUNZAKO
Bungwe la anthu a mtundu wa a MANG’ANJA lati liri mkati mokonza dongosolo lofuna kukhaka ndi msonkhano waukulu wa anthu a mtundu-wu m'dziko muno. M’modzi mwa akuluakulu a bungweli m’dziko muno a PULENI...
View ArticleANA ASUKULU ASAFIKE NTHAWI YOTSEKULIRA SUKULU ALI KU TSIMBA
Ofesi ya zamaphunziro m’boma la Balaka yati chaka chino iwonetsetsa kuti ana omwe alowe zinamwali, asakhale akadali kutsimba sukulu ikatsekulidwa mchigawo choyamba cha maphunziro a chaka chino mpaka...
View ArticleMEC IKHAZIKITSA NDONDOMEKO YA CHISANKHO CHA 2014
Bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission MEC latsimikizira anthu kuti ligwira ntchito yake mwa ukadaulo komanso mwachilungamo m’dziko muno. Wampando wa bungweli Justice...
View ArticleKWAYA ZIZAMITSE LUSO LOPEKA NYIMBO KUCHOKERA M'BUKU LOYERA
M’modzi mwa akatswiri poyimba nyimbo za uzimu m’dziko muno, PAUL BANDA wati mayimbidwe mu mpingo wakatolika, angapite patsogolo komanso kuyenda bwino, pokhapokha magulu oyimba mu mpingowu atazamitsa...
View ArticleAMAI A CHITEMWANO ACHEZERA ASEMINO KU KACHEBERE SEMINARY
Achinyamata omwe ali pamaphunziro aunsembe ku sukulu ya Kachebere m’boma la Mchinji, ayamikira gulu la amai la Chitemwano la mparishi ya St Denis ya mpingo wakatolika mudayosizi ya Mzuzu yampingowu,...
View ArticleUMOYO PATSOGOLO
Sabata yathunthu yoganizira zaumoyo,yayamba lero mdziko muno pamene zipatala zalimbikitsa ntchito yopereka katemera wa Ana ndi zithandizo zina kwa ana osaposera zaka zisanu. Pothilirapo ndemanga...
View ArticleAPHUNGU AKUNYUMBA YA MALAMULO AYAMBA KUVOMERA KAPENA KUKANA BUDGET
Aphungu akunyumba yamalamulo masana ano ayamba kuvomera kupena kukana ndondomeko yazachuma yomwe nduna yazachuma idapereka kunyumbayo pa 24 mwezi watha.Pamkumanowu aphunguwa akhala akukana kapena...
View ArticleCCJP IPHUNZITSA ZA KUSAMALIRA CHILENGEDWE
Bungwe la Catholic Commission for Justice and Peace mu arkdayosizi ya LILONGWE, lati ngati dziko lino silikhala tcheru ndikulimbikitsa mchitidwe osamalira zachilengedwe, lidzakumana ndizovuta zambiri...
View ArticleNAPHAM IKONDWA NDI MAMEMBALA AKE KU MANGOCHI
Bungwe la National Association for People Living with HIV and AIDS (NAPHAM) m’boma la MANGOCHI lati ndi lokondwa kuti ena mwa mamembala ake ayamba kuchita bwino pa miyoyo yawo kamba kotsatira bwino...
View ArticlePALIBE CHISANKHO CHACHIBWEREZA MU 2014 -MEC
Bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno, la Malawi Electoral Commission,lati silidaike tsiku lodzachitira chisankho chachibwereza m'ndondomeko yakagwiridwe ka ntchito zake zokonzekera chisankho cha...
View ArticleMAFUMU ALI NDI UDINDO WOLIMBANA NDI MCHITIDWE WOZEMBETSA ANA
Bungwe losamalira ana la Chisomo Childrens Club lati lipitiriza kudzipereka polimbana ndi mchitidwe ozembetsa ana m'madera osiyanasiyana mdziko muno. Bungweli lanena izi m’boma la Dedza pamsonkhano...
View ArticleMWAMUNA WINA ALAMULIDWA KUKHALA KUNDENDE ZAKA 8 ATABA MATUMBA 202 A FETEREZA
Bwalo la milandu la magistrate m'boma la Ntchisi lalamula mwamuna wina wa zaka 27, kuti akakhale kundende zaka zisanu ndi zitatu (8), atapezeka olakwa pa mlandu woba fetereza ndi mbewu za ndalama...
View ArticleATSOGOLERI ALEPHERA PA CHUMA - JUBILEE 50 MOVEMENT
Gulu lina la achinyamata lomwe langokhazikitsidwa kumene la JUBILLEE 50 MOVEMENT, lati atsogoleri omwe akhala akulamulira dziko lino alephera kukwaniritsa kukweza ntchito za chuma m'dziko muno....
View Article