Mtsogoleri wa Dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika Ayendera Nyumba...
Mtsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika, anakhala nawo pantchito yoyendera nyumba zomwe zikuyenera kugumulidwa kapena kukonzedwanso mumzinda wa Blantyre. Pulezidenti Mutharika,...
View ArticleBungwe la CCJP mu Diocese ya Dedza Lidzudzula Miyambo Yomwe Imakolezera...
Bungwe la Chilungamo ndi Mtendere mu Diocese ya Dedza lati zikhalidwe komanso miyambo ya Angoni imene ikuthandizira kufala kwa kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ka HIV ingatheretu mafumu...
View ArticlePapa Francisco Akhala Akupempherera Amayi Mmwezi wa March
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wati mwezi uno akhala akupempherera amayi mu mpingowu mwapadera ndi cholinga choti anthu azizindikira gawo lalikulu lomwe iwo amatenga...
View ArticleAna Osamva ndi Osalankhula Apambana pa Mpikisano
Sukulu ya ana omwe ali ndi vuto losamva komanso kusalankhula ya Mua School for the Deaf m’boma la Dedza,yayamikira ana apasukuluyi chifukwa chopambana kuposa anzawo a mmayiko ena pa mpikisano womwe...
View ArticleKikwete Athana ndi Vuto la Kuphedwa kwa Alubino
Mtsogoleri wa dziko la Tanzania Jakaya Kikwete,walonjeza kuti athana ndi vuto la kuphedwa kwa anthu omwe ali ndi khungu la alubino lomwe akuti lakula kwambiri mdzikolo. Polankhula pa wailesi ya kanema...
View ArticlePULOGALAMU YAPADERA YOFOTOKOZA ZA KUTULA PANSI UDINDO KWA PAPA BENIEIKITO WA...
Pulogalamu yapadera ndi Bambo Joseph Kimu
View ArticleMpingo wa Katolika Wakhazikitsa Ntchito Yopereka Thandizo
Ngati njira imodzi yosonyeza kukhudzidwa ndi mavuto amene anagwera anthu ambiri mdziko muno kamba ka ngozi ya kusefukira kwa madzi mpingo wakatolika lero wakhazikitsa ntchito yopereka thandizo kwa...
View ArticleBungwe la Partners In Health lati lidzipereka pa Chisamaliro cha Amayi ndi Ana
Bungwe lothandiza anthu pa nkhani za umoyo ndi kadyedwe kabwino la Partners in Health lati lidzipereka powonetsetsa kuti amayi oyembekezera ndi ana akulandira chisamaliro chabwino pa miyoyo yawo....
View ArticleMpingo wa Katolika Walimbikitsa za Kuthetsa Lamulo Lonyonga
Mpingo wa katolika ku Vatican wabwereza kupempha mayiko pa dziko lonse kuti athetse lamulo la kupha kwa anthu olakwira malamulo. Kazembe wa mpingowu ku bungwe la m’gwirizano wa maiko la United Nations...
View ArticlePapa Francisco ndi Wokhudzidwa ndi Mchitidwe Wogulitsa Mankhwala Ozunguza Bongo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndiwokhudzidwa ndi kuchuluka kwa anthu omwe amachita malonda ogulitsa mankhwala ozunguza bongo. Papa Francisco amalankhula izi...
View ArticleSimone Gbagbo Amulamula kuti Akakhale ku Ndende kwa Zaka 20
Mkazi wa mtsogoleri wakale wa dziko la Ivory Coast Simone Gbagbo, amulamula kuti akakhale ku ndende kwa zaka makumi awiri kamba kopezeka olakwa pa mlandu okolezera zipolowe pakusamvana komwe kunabuka...
View ArticleMpingo wa Katolika ndi Wokhudzidwa ndi Nkhondo ya Mdziko la Iraq
Mpingo wa katolika mdziko la Iraq, wati ndi wokhudzidwa ndi mavuto omwe anthu akukumana nawo mdzikolo pa nkhondo yomwe ilipo pakati pa asilikali a boma ndi zigawenga za Islamic State. Wapampando wa...
View ArticlePapa Francisco Akuyembekezeka Kukacheza Mdziko la CAR
Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco akuyembekezeka kukacheza mdziko la Central African Republic mmwezi wa November chaka chino. Pothilirapo ndemanga zaulendowu, Archepiskopi...
View ArticleAnsembe Akhale Odzipereka mu Nyengo Ino ya Lenti
Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco, wapempha ansembe kuti azidzipereka kwa akhristu awo amene akufuna kulapa, maka munyengo ino ya Lenti. Papa Francisco wapereka pempholi...
View ArticleAna 80 omwe Apulumutsidwa ku Gulu la Boko Haram, Sakukumbukira Mayina Awo ndi...
Ana pafupifupi makumi asanu ndi atatu omwe awapulumutsa ku gulu la zigawenga za Boko Haram mdziko la Nigeria, ati akulephera kukumbukira mayina awo komanso kwawo kochokera. Malipoti a mmodzi mwa anthu...
View ArticlePapa Francisco Wadzudzula Mayiko omwe Amalipira Aphunzitsi Malipiro Ochepa
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, wadzudzula mayiko omwe amapereka malipiro ochepa kwa aphunzitsi mmayiko awo. Papa Francisco wati kulipira aphunzitsi malipiro ochepa...
View Article