Bungwe la Landnet Lapempha Boma Kukhazikitsa Lamulo Lokhudza Malo
Bungwe la Landnet Malawi lapempha boma kuti likhazikitse msanga lamulo lokhudza malo lomwe aphungu akhala akulephera kulikambirana kunyumba ya malamulo, pofuna kuchepetsa milandu yokhudza malo mdziko...
View ArticleApolisi Aletsa Ziwonetsero Zomwe Akatolika Anakonza Mdziko la India
Apolisi mu mzinda wa New Delhi mdziko la India,aletsa ziwonetsero zomwe akhristu a mpingo wakatolika anakonza mumzindawo pokwiya ndi ziwembu zomwe anthu ena akumachitira matchalitchi a mpingowu...
View ArticleDayosizi ya Zomba Ikufufuza Njira Zofuna Kupeza Thandizo Lothandizira Anthu...
Pofuna kupeza thandizo lokwanira lopita kwa anthu omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira potsatira pempho la maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko muno,dayosizi ya Zomba ya mpingowu, yati ikufufuza njira...
View ArticleAnthu Akhale ndi Nthawi Yapadera Yoyendera Odwala
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco,wapempha anthu kuti pamene mpingowu lachitatu umakumbukira odwala padziko lonse, akhale ndi nthawi yapadera yoyendera odwala, pofuna...
View ArticleMutharika Akhaziktsa Ndondomeko za Kayendetsedwe ka Ntchito za Boma
Mtsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika, wakhazikitsa ndondomeko zomwe zithandize nthambi zaboma kuyendetsa bwino ntchito zake. Polankhula pa mwambo okhazikitsa ndondomekoyi ku Bingu...
View ArticleLikulu la Mpingo wa Katolika ndi Lokhudzidwa ndi Kukwera kwa Chuma
Likulu la mpingo wakatolika ku Vatican, lawuza bungwe la mgwirizano wa mayiko la United Nations,kuti mpingowu ndiwokhudzidwa kwambiri powona kuti kukwera kwa chuma mmayiko ena padziko lonse,...
View ArticleBungwe la Community of Saint Egidio Likondwelera Zaka 47 Chilikhazikitsire
Bungwe la Community of Saint Egidio lati ndi lokondwa kuti tsopano lakwanitsa zaka 47 kuchokera pomwe bungweli linayamba kugwira ntchito zake zolimbikitsa moyo wa mapemphero ndi kudzipeleka pogwira...
View ArticleBambo Corna a Mdziko la Italy Amwalira
A ku Likulu la chipani cha Mofolo Woyera ku Rome mdziko la Italy alengeza za imfa ya Bambo Attilio Corna omwe anamwalira lachiwiri pa 10 February 2015 mu mzinda wa Bergamo mdzikolo. Bambo Corna...
View ArticleSister Martha Clemence Manuel Makhasa a Chipani cha SBVM Amwalira
Sister Martha Clemence Manuel Makhasa a Chipani cha Servants of Blessed Virgin Mary (SBVM), amwalira lachisanu. Malinga ndi akulikulu la chipanichi Sister Martha anabadwa pa 8 September 1932 ndipo...
View ArticleAmbuye Musikuwa Ayamikira Mabungwe ndi Anthu Akufuna Kwabwino Chifukwa Cha...
Dayosizi ya Chikwawa yayamikira mabungwe ndi anthu akufuna kwabwino omwe akuthandiza dayosiziyi ndi ndalama komanso zinthu zosiyanasiyana zothandizira anthu omwe akuvutika ndi kusefukira kwa madzi ....
View ArticleZigawenga za I.S Zanyonga Akhristu Makumi Awiri
Zigawenga za mgulu la Islamic State I.S, zalengeza kuti zanyonga akhristu makumi awiri ndi mmodzi a mdziko la Egypt,omwe zidawagwira mdziko la Libya kumayambiliro a mwezi wa January chaka chino....
View ArticleAnthu asanu ndi awiri afa ndi Bomba
Anthu asanu ndi awiri afa mayi wina ataphulitsa mabomba pamalo ena okwelera bus mumzinda wa Damaturu mdziko la Nigeria. Malipoti a apolisi ati pachiwembucho,anthu makumi atatu 30,avulala. Padakali...
View ArticleMa Sisteri Awiri a Chipani cha SBVM Ayikidwa Mmanda
Mwambo woyika mmanda asisteri awiri Sister Chrissy Govati ndi Sister Martha Clemence Manuel Makhasa a Chipani cha Servants of the Blessed Virgin Mary wachitika lolemba ku Mary View ku Nguludi mu...
View ArticleMpingo wa Katolika Wafunira Akhristu Zabwino mu Nyengo ya Lenti
Mpingo wakatolika kuno ku Malawi wafunira akhristu komanso a malawi onse mafuno abwino,pamene lero ayamba ulendo wa masiku makumi anayi okumbukira masautso a Yesu Khristu. Polankhula ndi Radio Maria...
View ArticlePapa Francisco Alimbikitsa Achinyamata Kuzamitsa Moyo wa Uzimu
Muuthenga wachaka cha achinyamata chaka chino, mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, wapempha akhristu mumpingowu kuti azamitse moyo wawo wauzimu poyeretsa mitima yawo....
View ArticleZigawenga za Boko Haram Zilepheretsa Zisankho Mdziko la Nigeria
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga za Boko Haram Abubakar Shekau, wanenetsa kuti alepheretsa zisankho za atsogoleri zomwe dzikolo likuyembekezeka kukhala nazo pa 28 March chaka chino. Iye wanena izi...
View ArticleMpingo wa Katolika ku Vatican Uganizira Anthu Osowa
Mpingo wa katolika ku Vatican wakhazikitsa malo ometera awulele a anthu osowa kwawo. Pa mwambowu womwe unatsekuliridwa ndi mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco kunafika anthu...
View ArticleApempha Mafumu Kuchita Chilungamo Polemba Maina Aanthu Osowa Thandizo.
Bungwe lachitukuko mumpingo wakatolika la Cadecom mu dayosizi ya Mangochi,lapempha mafumu, kuti azichita chilungamo polemba mayina a anthu oyenera kulandira thandizo pa ngozi ya madzi osefukira yomwe...
View ArticleAkristu a ku Middle East Ali Pamavuto Aakulu.
Mpingo wa Katolika mdziko la Greece wati akhristu a mmayiko a ku Middle East, atha zaka zisanu tsopano ali pamavuto aakulu kaamba ka nkhondo yomwe ili mmayikowo. Bishop Gregory Laham,ndi yemwe wanena...
View ArticleNyengo ya Lent Nthawi Yowonjezera Mphanvu Zolimbana ndi Mkhalidwe Wauchimo.
Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco, wati nyengo ya Lenti ndi nthawi yowonjezera mphamvu zolimbana ndi mkhalidwe wauchimo. Papa Francisco, wanena izi la Mulungu pamapemphero a...
View Article