TIME TO TAKE ACTION TO STOP THE KILLINGS OF ALBINOS IN MALAWI
CATHOLIC COMMISSION FOR JUSTICE AND PEACE OF THE EPISCOPAL CONFERENCE OF MALAWI TIME TO TAKE ACTION TO STOP THE KILLINGS OF ALBINOS IN MALAWI “Media statement in solidarity...
View ArticlePapa Ali Limodzi ndi Anthu a Mdziko la Nigeria
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco,watsimikizira maepiskopi a mdziko la Nigeria kuti ali nawo limodzi pamavuto osiyanasiyana omwe dziko lawo likukumana nawo. Iye wanena izi...
View ArticleBOMA LIFUFUZA ANTHU OMWE ANATUMA ANA KUTI ACHITE ZIONETSERO
Boma la Malawi lati lifufufuza ndi kumanga anthu omwe adatsogolera ana a sukulu omwe adachita ziwonetsero zokwiya ndi kuima kwa maphunziro pamene aphunzitsi mumzinda wa Blantyre amachita nawo...
View Article"MUKHALE ZITSANZO ZABWINO", BAMBO MULAVA
Abwenzi a Radio Maria awapempha kukhala zitsanzo zabwino pokondana ndi kulimbikapogwira ntchito zothandiza wayilesiyi. Wachiwiri kwa wamkulu owona za ma Pulogalamu ku wayilesiyi, Bambo Medrick Mulava...
View ArticleBungwe la CADECOM Layamikira Boma Pokhazikitsa Ndondomeko Zabwino za Ngozi...
Bungwe lowona zachitukuko mu mpingo wakatolika la Catholic Development Commission CADECOM mdziko muno, layamikira boma kamba kokhazikitsa ndondomeko zomwe zithandize dziko lino kulimbana komanso...
View ArticlePapa Francisco Wayamikira Akhristu aku Japan Chifukwa cha Chikhulupiliro...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco,wayamikira akhristu a mpingowu mdziko la Japan chifukwa cholimba pa chikhulupiliro chawo,ngakhale akhala akukumana ndi mavuto osiyanasiyana...
View ArticleDZIKO LA TANZANIA LIFUFUZA ZA KUPHEDWA KWA WAMSEMBE
Pulezidenti wa dziko la Tanzania a Jakaya Kikwete walamula apolisi m’dzikolo kuti afufuze mwansanga za kuphedwa kwa wamsembe wina wa Mpingo wa Katolika m’dzikolo. Pulezidenti Kikwete walamula izi...
View ArticlePulezident Jonathan Asayinira Mgwirizano ndi a Buhari
Pulezidenti Goodluck Jonathan ndi yemwe anali mkulu wa asilikali a gulu la nkhondo a dziko la Nigeria a Muhammadu Buhari asayinirana mgwirizano wakuti sipadzakhala ziwawa pambuyo pa zotsatira za...
View ArticleMa Episkopi Makumi Anayi ndi omwe Akakhale Nawo pa Msonkhano Wachiwiri...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, wavomereza mayina a maepiskopi a mmayiko makumi anayi omwe mabungwe a maepisikopi mmayikowa asankha kuti akawayimilire pa msonkhano...
View ArticlePapa Francisco Wapepesa Mabanja omwe Akhudzidwa ndi Ngozi ya Ndege
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, wapepesa mabanja omwe ataya abale awo pangozi ya ndege yomwe yachitika lachiwiri mdziko la France. Ndegeyo yomwe ndi ya mdziko la Germany,...
View ArticleNyumba Zofalitsa ndi Kutsindikiza Nkhani Zili ndi Udindo Wofalitsa Nkhani za...
Unduna wa zaumoyo wati nyumba zofalitsa komanso kutsindikiza nkhani zili ndi udindo waukulu wofalitsa nkhani zokhudza matenda osiyanasiyana m’dziko muno. Nduna mu undunawu Wolemekezeka Dr Jean Kalirani...
View ArticleBungwe la Cadecom Layamikira Bungwe la YCW
Bungwe lowona za chitukuko mu mpingo wa Katolika la Cadecom, layamikira achinyamata a mgulu la YCW mu Parish ya Kaggwa Woyera ku Archdayosizi ya Lilongwe popereka katundu wosiyanasiyana ku bungweli...
View ArticlePapa Francisco Akumana ndi Barrack Obama Mwezi wa September
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco akuyembekezeka kukumana ndi mtsogoleri wa dziko la America Barrack Obama mwezi wa September chaka chino. Paulendowu Papa Francisco...
View ArticleUnduna wa Zaumoyo Walimbikitsa Anthu kuti Apewe Matenda a Makutu
Unduna wa zaumoyo walangiza anthu mdziko muno kuti apewe mchitidwe omvera zinthu zomwe zikupereka phokoso lopitilira muyeso pofuna kupewa matenda a khutu. Nduna ya za umoyo Dr. Jean Kalirani ndi yomwe...
View ArticleA Mipingo Atengepo Gawo Lolimbana ndi Matenda a Edzi
Bungwe la atolankhani lolimbana ndi matenda a Edzi la Journalist Against Aids, lati matendawa m’dziko muno angachepe ngati a mipingo atadzipereka pofalitsa kuopsa kwa matendawa akakhala m’makachisi...
View ArticleChipatala cha Bwaila Fistula Care Centre Achiyamikira Pokwaniritsa Zina mwa...
Chipatala chomwe chimathandiza amayi omwe anapezeka ndi vuto la Fistula cha Bwaila Fistula Care Centre mu mzinda wa Lilongwe, achiyamikira kamba kokwaniritsa zina mwa zolinga zake polimbana ndi vutoli....
View ArticleAkhristu Atsatire Makhalidwe a Yesu Khristu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wati akhristu angathe kupewa mayesero a dziko lapansi potsatira makhalidwe omwe Yesu Khristu mwini adawonetsa. Papa Francisco wanena izi...
View ArticleAkhristu Akhale Olimba pa Chikhulupiriro Chawo
Akhristu awalangiza kuti akhale olimba pa chikhulupiliro pofuna kuti azitha kugonjetsa adani achikhulupiriro chawo. Mmodzi mwa ansembe otumikira ku Seminary ya Nankhunda mu dayosizi ya Zomba ya mpingo...
View ArticleMapemphero Ati ndi Chida Chothandizira Aphunzitsi Kugwira Ntchito Yawo
Mapemphero ati ndi njira yokhayo yomwe ingathandize aphunzitsi kugwira ntchito yawo yophunzitsa ndi kulangiza ana a sukulu pa nkhani yokhudza umoyo wa thupi ngakhalenso wa uzimu posayang’anira mavuto...
View Article