MWANA WAZAKA 6 WAMIRA KU NKHOTAKOTA
Apolisi mboma la Nkhotakota ati mwana wa zaka zisanu ndi chimodzi wamira mumtsinje wa Dwangwa m’mudzi mwa Denja mfumu yayikulu Kanyenda mbomalo. Malinga ndi mneneri wa apolisi ya Nkhunga Labani...
View ArticleVUTO LA MADZI LAFIKA POYIPA PA CHIPATALA CHA MWANZA
Ntchito za umoyo zayima pa chipatala cha boma la Mwanza kamba ka vuto la madzi pomwe odwala akutha masiku anayi asanasambe. Malinga ndi zomwe Radio Maria yapeza, anthu odikirira odwala pachipatalacho...
View ArticleMPINGO WA KATOLIKA KU MALAWI UWUNIKIRA ANTHU PA ZA CHISANKHO
Pamene kwangotsala miyezi iwiri kuti dziko la Malawi lichite zisankho zake zoyamba za patatu pa 20 May bungwe lampingo wakatolika la chilungamo ndi mtendere la CCJP latulutsa chikalata chomwe muli...
View ArticleMmene mumandikondera
Mmene mumandikondera, St Annie Choir, St Francis Knengo Parish, Lilongwe Archdiocese
View ArticleAmbuye mutitsogolere
Ambuye mutitsogolere by Montfort Media Choir Mangochi diocese [ ya chisankho]
View ArticleMdima unadetsa dziko
Mdima unadetsa dziko by Lunzu Catholic Women Choir, Blantyre Archdiocese
View ArticleAdampachika pa mtandapo
Adampachika pa mtandapo by Utatu woyera choir, Mua Parish Dedza Diocese
View ArticleAdampachika pamtandapo
Adampachika pamtandapo by Utatu oyera choir Mua parish Dedza diocese
View ArticleAMBUYE SITIMA AYENDERA LIKULU LA RADIO MARIA MALAWI
Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi yampingo wakatolika Ambuye Montfort Sitima ati adzipeleka kothelatu pa ntchito zothandiza komanso kutumikira Radio Maria Malawi. Episikopiyu amayankhula izi pomwe kwa...
View Article