ANTHU AWIRI AMWALIRA PA NGOZI KU NENO
Anthu awiri amwalira lolemba pa ngozi ziwiri zogundidwa ndi galimoto mboma la Neno. Malinga ndi mneneri wa apolisi mbomalo a Raphael Kaliati, ngozi yoyamba inachitikira pa msika wa Kanono koma bambo...
View ArticleBAMBO MATTIAS CHIWANDA AMWALIRA
M’modzi mwa amsembe ampingo wakatolika mu dayosizi ya Chikwawa bambo Mattias George Chiwanda amwalira lachiwiri madzulo atadwala kwa nthawi yochepa. Malinga ndi akulikulu la mpingo wakatolika kuno ku...
View ArticleMONSINYO VAN MEGEN NDI NDUNA YATSOPANO YA PAPA KU SUDAN
Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wasankha yemwe anali oyimilira Papa kuno ku Malawi Mosinyo Hubertus Matheus Maria van Megen kukhala nduna yatsopano ya Papa mdziko la...
View ArticleMPINGO WAKATOLIKA WATI OYAMBITSA ZIWAWA ALANDIRE CHILANGO
Bungwe la Catholic Commission for Justice and Peace [CCJP] lomwe ndi nthambi ya bungwe la ma episkopi ampingo wakatolika kuno ku Malawi lapempha bungwe loona za chisankho la Malawi Electoral Commission...
View ArticleAdampachika pa mtandapo
Adampachika pa mtandapo by st marys catholic choir kamuzu barracks
View ArticleBAMBO CHIWANDA ALOWA M’MANDA
Ma episkopi atatu ampingo wakatolika kuno ku Malawi lachinayi pa 20 march anatsogolera anthu zikwizikwi pa mwambo woyika m’manda thupi la bambo Matthias Chiwanda amu dayosizi ya Chikwawa omwe...
View ArticleANTHU ATATU AMWALIRA PA NGOZI KU MZUZU
Anthu atatu kuphatikizapo msungwana wa zaka khumi ndi zitatu amwalira atawombedwa ndi galimoto pa mtsinje wa Lunyangwa mumsewu wa Mzuzu-Karonga loweruka. Malinga ndi mneneri wa apolisi mumzinda wa...
View ArticleAKHRISTU 23 APITA KU MALO OYERA KU ROME MWEZI WA MAWA
Akulu akulu omwe akuyendetsa zokonzekela za ulendo wa akhristu a ku Malawi opita kumalo oyera ku Rome mdziko la Italy pa 16 April chaka chino ati zokonzekera za ulendowo zili mkati ndipo zikuyenda...
View ArticlePULEZIDENTI BANDA WATI A MUTHARIKA ANAYAMBITSA ZIWAWA KU THYOLO
Pulezidenti Dr Joyce Banda wati ziwawa zomwe zinachitika kwa Goliati mboma la Thyolo sabata yatha zomwe zinazetsa imfa ya wapolisi ndi munthu wamba m’modzi zinakonzedwa ndi pulezidenti wachipani cha...
View ArticleA MALAWI ALEMBA NAWO BAIBULO LA CHICHEWA PA MANJA
A Malawi akhala ndi mwayi olemba nawo Baibulo la Chichewa pa manja lomwe likasiyidwe ku malo omwe amasungirako ma Baibulo mdziko la Israel. Malinga ndi mkulu yemwe akuyendetsa ntchitoyi mdziko muno...
View ArticlePULEZIDENTI BANDA WAKHUTIRA NDI MMENE MALONDA A FODYA AYAMBIRA
Pulezidenti Dr Joyce Banda wati ndi okondwa ndi mitengo yomwe alimi anagulitsira fodya wawo lolemba pamene amatsekulira msika wambewuyi chaka chino ponena kuti akukhulupirira kuti chaka cha 2014...
View ArticleMABUNGWE AKWIYA NDI KUYIMITSIDWA KWA NTCHITO YOWUNIKA MAYINA MKAWUNDULA
Anthu komanso mabungwe omwe sia boma ati sakugwirizana ndi zomwe bungwe la za chisankho la MEC lachita poyimitsa ntchito ya mugawo loyamba lowunika mayina mukawundula wa voti yomwe inayamba lolemba...
View ArticleA PAYONIYA AKUFUNA CHILUNGAMO KUCHOKERA KU BOMA
Mamembala a gulu lakale la boma la Malawi Young Pioneers [MYP] lachiwiri anakatula chikalata kwa pulezidenti Joyce Banda kudzera ku ofesi ya bwanamkubwa wa mboma la Lilongwe chopempha kuti alowererepo...
View ArticleMA BISHOPU AMPINGO WA ANGLICAN APEMPHA KAMPENI YA BATA
Pomwe mabungwe ndi zipembezo zikupitiriza kudzudzula mchitidwe wa ziwawa womwe unaphetsa wapolisi ndi munthu wamba m’modzi kwa Goliati mboma la Thyolo mpingo wa Anglican wapempha boma kuti lionetsetse...
View ArticleDAYOSIZI YA MANGOCHI IKUZINDIKIRITSA ACHINYAMATA ZOPEWA ZIWAWA
Pamene kwangotsala sabata zowerengeka kuti anthu adzaponye voti pa chisankho cha patatu pa 20 May, Dayosizi ya Mangochi yampingo wakatolika yati ikudzipereka powonetsetsa kuti chisankhochi...
View Article