Ndewu Pakati Pa Njoka ndi Chule
Ulaliki titled Ndewu Pakati Pa Njoka ndi Chule by Father James Chizuma
View ArticleNZIKA ZILI NDI UDINDO PA ZISANKHO ZA 2014-MEC
Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC), lati nzika za m’dziko lino zikuyenera kuonetsa udindo wawo potenga mbali pazisankho zachaka cha mawa polembetsa m’nkaundula wa mavoti. Wapampando wa bugweli...
View ArticleA CCJP media statement in total condemnation of the resurgence of the...
1.0. Preamble The Catholic Commission for Justice and Peace (CCJP) of the Episcopal Conference of Malawi is a social justice and advocacy arm of the Catholic Church in Malawi that is...
View ArticleMfumu Zwelithini ya Mdziko la South Africa Ikuyembekezeka Kudzudzula Anthu...
Mfumu yachizulu Good-will Zwelithini ya mdziko la South Africa ikuyembekezeka kulankhulapo popempha mzika za dzikolo kuti zisiye kuchitira mtopola mzika za mmayiko ena zomwe zikukhala mdzikolo pa...
View ArticleAnthu Achitepo Kanthu Pofuna Kuchepetsa Imfa za pa Nyanja
Mtsogoleri wampingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha mayiko padziko lonse kuti achitepo kanthu pofuna kuchepetsa imfa za anthu omwe akumwalira panyanja, paulendo opita mmayiko a ku...
View ArticleBungwe la Law Society ndi lokhudzidwa ndi Mavuto omwe Dziko Lino Likukumana Nawo
Bungwe lowona za malamulo mdziko muno la Law Society lati ndi lokhudzidwa kwambiri ndi mavuto omwe dziko lino layamba kukumana nawo posachedwapa pankhani zosiyanasiyana. Ena mwa mavuto omwe bungweli...
View ArticleMESSAGE FOR VOCATION SUNDAY – 26 APRIL 2015
Theme: Do not be afraid, God does not abandon us Dear Brothers and Sisters in the Lord, The Fourth Sunday of Easter, which is the Good Shepherd Sunday, 26thApril 2015 is Vocation Sunday. It is a...
View ArticleApereka nthandizo kwa Amayi Oyembekezera
Wapampando wa bungwe la achinyamata ku mphakati wa St Teleza ku parish ya St Francis mu Archdiocese ya Lilongwe a Kodwani Cornelius Zalimba, wati achinyamata m’dziko muno akuyenera kusintha makhalidwe...
View ArticleDziko la Malawi Lisainira Mgwirizano wa Za Malonda
Mgwirizano wa malonda omwe wachitika pakati dziko lino ndi dziko la Tanzania, akuti uthandiza kwambiri pa chitukuko cha za malonda m’dziko muno. Nduna ya za malonda ndi mafakitale olemekezeka a Joseph...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Iyamikira Akhristu
Dayosizi ya Mangochi ya mpingo wa Katolika yayamikira akhristu a mpingowu komanso anthu akufuna kwabwino a mu dayosizi ya Zomba ndi Dedza, kamba kopereka thandizo la chakudya ndi zovala kwa anthu omwe...
View ArticleMorsi Amulamula kuti Akakhale ku Ndende Zaka 20
Yemwe kale adali m’tsogoleri wa dziko la Egypt a Mohamed Morsi amulamula kuti akakhale kundende ndi kukagwira ntchito yakalavulagaga kwa zaka makumi awiri 20 kamba komupeza wolakwa pa milandu...
View ArticleLikulu la Mpingo Wa Katolika Lasayinirana Mgwirizano ndi Bungwe la United...
Likulu la mpingo wa Katolika pa dziko lonse ndi nthambi ya bungwe ya United Nations yosamalira ana asayinirana pangano logwilira ntchito limodzi pofuna kuthandiza achinyamata osowa pa dziko lonse....
View ArticleBungwe la Save the Children Lapempha Mayiko kuti Ateteze Anthu omwe Akumafa...
Bungwe lowona za chisamaliro cha ana la Save the Children lati ana pafupifupi 2, 500 amwalira pomafika kumapeto a chaka chino, ngati mayiko aku Ulaya sadzipereka poteteza anthu omwe akumafa pa ngozi za...
View ArticleBungwe la Prison Fellowship of Malawi Lasayinila Pangano ndi Malawi Prison...
Bungwe lomwe limapereka luso losiyanasiyana kwa anthu omwe atuluka kundende la Prison Fellowship of Malawi la m’boma la Balaka, lachisanu lasayinirana pangano ndi nthambi yoyendetsa ndende za mdziko...
View ArticleApolisi Mdziko la France Akhwimitsa Chitetezo Mmatchalitchi Akatolika
Malo 178 a mpingo wa Katolika mdziko la France kuphatikizapo matchalitchi, akuyembekezeka kutetezedwa ndi apolisi zitadziwika kuti gulu lazauchifwamba la mdziko la Syria limakonza zochita zamtopola...
View ArticleMayiko aku Ulaya Awonjezera Thandizo Lolimbana ndi Anthu Olowa Mmayiko ena...
Atsogoleri a mayiko akuulaya amvana zowonjezera thandizo lomwe amapereka pa ntchito yolimbana ndi anthu a mmayiko ena omwe amalowa mayikowo mosavomerezeka pogwiritsa ntchito mabwato. Atsogoleriwa...
View ArticleOPHUNZIRA MSUKULU ZOSIYANASIYANA APHUNZITSIDWE ZA CHILENGEDWE
Unduna woona zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo wati ugwira ntchito ndi unduna wa zamaphunziro ndi cholinga choti ophunzira m’sukulu zosiyanasiyana aziphuzitsidwa mokwanira momwe angamasamalire...
View ArticleMutharika wati Amalawi Safa ndi Njala
Mtsogoleri wa dziko lino Proffessor Arthur Peter Mutharika walonjeza amalawi kuti palibe amene akumane ndi vuto la kusowa kwa chakudya chaka chino. Mtsogoleriyu walankhula izi lachiwiri pa msonkhano...
View ArticleAsilikali a Dziko la Nigeria Apulumutsa Anthu 300 ku Zigawenga za Boko Haram
Asilikali a mdziko la Nigeria apulumutsa anthu pafupifupi mazana atatu omwe amasungidwa mu nkhalango ina ndi zigawenga za chisilamu za Boko Haram m’dzikomo. Anthuwa omwe mazana awiri ndi atsikana...
View Article