Bungwe la Maneb Lapempha Magulu kuti Adzipereke
Bungwe lowona za mayeso mdziko muno la National Examinations Board MANEB,lapempha magulu osiyanasiyana kuti adzipereke powonetsetsa kuti vuto lobera mayeso lipitilire kuchepa mdziko muno. Mkulu owona...
View ArticleZuma wati Dziko Lake ndi la Mtendere
Mtsogoleri wa dziko la South Africa Jacub Zuma wati anthu amene amachitira alendo ziwembu mdzikolo ndi ochepa kwambiri poyerekeza ndi anthu omwe amakonda mtendere. Pulezidenti Zuma wanena izi lachisanu...
View ArticleMa Episkopi Adzipereke pa Ntchito Yophunzitsa Anthu Nkhani Zokhudza Banja
Atsogoleri a mipingo yosiyanasiyana kuphatikizapo maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la America ati apitiliza kudzipereka pa ntchito yophunzitsa anthu nkhani zokhudza banja lapakati pa mwamuna ndi...
View ArticlePapa Francisco Ayamikira Asilikali pa Ntchito Yabwino
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira asilikali omwe amagwira ntchito ya chitetezo ku likulu la mpingowu ku Vatican pa ntchito yabwino yomwe amagwira. Papa...
View ArticleBungwe la NYD likhazikitsa Pulojekiti ya Chisankho cha Moyo Wanga
Pofuna kuwonetsetsa kuti atsikana ndi amayi akulimbikitsidwa pa ntchito yodziyimira pawokha, bungwe lomwe si laboma la Network for Youth Development likhazikitsa ndondomeko ya ndalama zokwana 25...
View ArticleAnthu Pafupifupi 6 Thousand Agwidwa pa Nyanja ya Mediterranean
Anthu oposa 5 sauzande 800,agwidwa mu nyanja ya Mediterranean sabata yapitayi, pamene anthu ogwira ntchito yowona zachitetezo cha anthu pa nyanjayo akhwimitsa chitetezo. Pantchitoyi achitetezowo, apeza...
View ArticleAnthu 137 Amila pa Nyanja ya Mediterranean
Malipoti akusonyeza kuti anthu 137 ndi omwe amwalira munyanja ya Mediterranean bwato lomwe anakwera litamira pa doko la Sicily mdziko la Italy. Malipoti a Wailesi ya BBC ati anthu makumi ndi anayi ndi...
View ArticleApolisi M’boma la Balaka Alangiza Woyendetsa Galimoto Kugwilitsa Tchito...
Apolisi m’boma la Balaka alangiza anthu oyendetsa galimoto kuti adzigwiritsa ntchito zizindikiro zapanseu pofuna kupewa ngozi. Apolisiwa apereka langizoli msungwana wazaka khumi ndi zitatu ndi bambo...
View ArticlePapa Francisco Akuyembezeka Kukumana ndi Mtsogoleri wa Dziko la Cuba
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco, akuyembekezeka kukumana ndi Pulezidenti wa dziko la Cuba a Raul Castro ku likulu la mpingowu la Mulungu likudzali. Malinga ndi uthenga...
View ArticleAnthu Anayi Afa Mdziko la Burundi
Anthu anayi aphedwanso pa ziwawa zomwe zikuchitika mdziko la Burundi pamene anthu akumbali yotsutsa boma akukana kuti mtsogoleri wa dzikolo ayimenso kachitatu pachisankho chomwe chichitike mdzikolo...
View ArticleMzimayi Ataya Mwana Patchire
Apolisi m’boma la Dowa amanga mayi wazaka makumi anayi ndi chimodzi 41, yemwe ndi m’busa wa mpingo wa Assemblies of God ku Mvera m’bomalo chifukwa chotaya mwana wake patchire atangobadwa kumene....
View ArticlePapa Francisco Wayamikira Mgwirizano wa Pakati pa Zipembedzo
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wayamikira mgwirizano omwe ulipo pakati pa zipembedzo padziko lonse. Papa Francisco,amalankhula izi lachinayi pa msonkhano wa akuluakulu a...
View ArticlePRESS RELEASE
NATIONAL CELEBRATION OF YEAR OF CONSECRATED LIFE: MAULA PARISH Saturday 16th May 2015 The Catholic Church in Malawi has joined the rest of the Catholic faithful in the world in celebrating the...
View ArticleDayosizi ya Zomba Yapempha Anthu Akufuna Kwabwino kuti Athandize RMM Zomba...
Ofesi yofalitsa nkhani mu dayosizi ya Zomba yapempha anthu akufuna kwabwino kuti athandize dayosiziyi ndi zipangizo zogwilira ntchito ku studio ya Zomba ya Radio Maria ndi cholinga choti dayosiziyi...
View ArticlePapa Alimbikitsa ma Episkopi a Mdziko la Mozambique kuti Akhale pa Ubale...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco walimbikitsa maepiskopi a mdziko la Mozambique kuti apitilize kukhala paubale wabwino ndi ansembe awo powathandiza pa zosowa za moyo wawo...
View ArticleBambo wina Apezeka Atafa M’boma la NtchisiBambo wina Apezeka Atafa M’boma la...
Bambo wina m’boma la Ntchisi wapezeka atafa mmudzi mwa Gamba kwa mfumu yayikulu Chilooko. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergent Gladson M’bumpha bamboyo anapezedwa ndi a Thokozani...
View ArticleGood Luck Jonathan Achenjeza Nduna Zake
Pamene dziko la Nigeria likuyembekezeka kulumbilitsa mtsogoleri watsopano kumapeto a mwezi uno, pulezidenti Good Luck Jonathan yemwe akuchoka paudindowu, wawopseza nduna zake kuti zizunzika kwambiri...
View ArticleMabungwe a Mpingo Wakatolika Ogwila Ntchito za Chifundo Ayamba Msonkhano Wawo...
Mabungwe 164 a mpingo wakatolika omwe amagwira ntchito zachifundo padziko lonse omwe adabwera pamodzi ndikupanga bungwe la Caritas International, lachiwiri ayamba msonkhano wawo wa pachaka pofuna...
View ArticleWogwirizira Kayendetsedwe ka Ntchito mu Dayosizi ya Zomba Wamwalira
Likulu la mpingo wakatolika mdziko muno lati ndi lokhudzidwa kwambiri ndi imfa ya Bambo mfumu a parishi ya Zomba Cathedral mu dayosizi ya Zomba Bambo Henry Kaleso omwe amwalira lachitatu masana....
View ArticleMonsignor Henry Kaleso Ayikidwa Mmanda
Mpingo wakatolika mdziko muno wati malemu Bambo Henry Kaleso omwe akhala akugwira ntchito zoyendetsa dayosizi ya Zomba, anali munthu odzipereka kwambiri pantchito zotumikira mpingo komanso anthu....
View Article