Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Ambuye Musikuwa Alimbikitsa Ansembe Ndi Akhristu Kukhala Odzipeleka...

Episkopi wa dayosizi ya Chikwawa ya mpingo wa Katolika wolemekezeka Ambuye Peter Musikuwa, wapempha ansembe ndi akhristu eni ake kuti azipempherera anthu amene akukumana ndi mavuto osiyanasiyana pa...

View Article


Mpingo Wakatolika ku Burundi Wapempha Mtsogoleri Wa Dzikolo Kuti...

Bungwe la ma Episkopi a mpingo wa Katolika m’dziko la Burundi lati silikugwirizana ndi zomwe m’tsogogoleri wa dzikolo akufuna kuti adzayimenso  pa chisankho cha president kamba koti matelemu ake...

View Article


Radio Maria Ikhazikitsidwa Mdziko la Madagascar

Akuluakulu oyendetsa ntchito za Radio Maria pa dziko lonse alengeza zakubadwa kwa wailesi ina m’dziko la Madagascar Kukhadzikitsidwa kwa wailesiyi kwachulukitsa  nambala ya mayiko amene ali ndi Radio...

View Article

Papa Francisco Achititsa Mwambo wa Wokhazikitsa Chifundo Cha Mulungu

Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco usiku wa pa 11 mwezi uno, adzachititsa mwambo wokhazikitsa chaka cha Chifundo cha Mulungu chomwe chidzayambe  mwezi wa December chaka...

View Article

Apempha Ma Parish kukhazikitsa tsiku Lopembedza Ambuye Yesu Mu Sacrament la...

Archepiskopi wa Archdiocese ya Blantyre Ambuye Thomas Luke Msusa wapempha atsogoleri a m’ma parishi kuti akhazikitse masiku apadera othandizira akhristu kucheza ndi Ambuye Yesu mu sacrament la...

View Article


Amayi a Mpingo Wakatolika ku St Martin Ku Chirimba Athandiza Anthu Okalamba...

Pamene akhristu mdziko muno akuchita chikondwelero cha kuuka kwa Yesu Khristu, amayi a mpingo wakatolika ku parish ya St Martin ku Chirimba mu Archdiocese ya Blantyre, anachita mwambo wotolera thandizo...

View Article

Anthu Akuchitidwa Chipongwe Chifukwa Chosowa Chipatala

Anthu okhala mdera la Kachere mu mzinda wa Blantyre adandaula chifukwa cha kusowa kwa Chipatala chaching`ono chothandiza anthu m’deralo, maka amayi omwe akuti amayenda mtunda wawutali akafuna thandizo...

View Article

Papa Francisco Wapempha Anthu Olemera kuti Azithandiza Anthu Ovutika

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu olemera kuti azitha kugawana zomwe ali nazo ndi anthu ovutika. Papa amalankhula izi  lachiwiri pa mwambo wa misa womwe...

View Article


Anthu 400 Amira pa Nyanya ya Mediterranean

Anthu pafupifupi 400 akuwaganizira kuti amira munyanja ya Mediterranean mdziko la Libya, boti lomwe anakwera litatembenuzika pomwe amafuna kulowa mmayiko aku ulaya kudzera pa Nyanja. Pa nthawi ya...

View Article


Dziko la South Africa Lamanga Anthu 17 ndi Kuwatsekulira Milandu Yakupha

Dziko la South Africa lamanga anthu 17 ndipo ena mwa iwo lawatsekulira milandu yakupha paziwawa zomwe mzika za dzikolo zikuchita pokwiya ndi anthu a mmayiko ena omwe akugwira ntchito zosiyanasiyana...

View Article

Ophunzira Mmodzi Wafa ndipo Ena Avulala Mdziko la Kenya

Ophunzira mmodzi wafa ndipo ena oposa zana limodzi, avulala pa sukulu ina ya ukachenjede  mu mzinda wa Nairobi m’dziko la Kenya, transifoma ya magetsi itaphulika pafupi ndi sukuluyo. Ophunzirayo wafa...

View Article

Chiwerengero cha Akhristu Akatolika Chakwera

Lipoti latsopano lomwe likulu la mpingo wakatolika latulutsa, lasonyeza kuti chiwerengero cha akhristu a mpingowu chakwera kwambiri mu zaka zisanu ndi zitatu zapitazi. Lipotilo lati kuyambira mchaka...

View Article

Anthu Zikwi Zisanu a Mdziko la South Africa Anachita Ziwonetsero

Anthu pafupifupi zikwi zisanu,mdziko la South Africa lachinayi anachita ziwonetsero zokwiya ndi ziwembu zomwe mzika zina za dzikolo zakhala zikuchitira anthu a mmayiko ena omwe akukhala mdzikolo....

View Article


Mwana wina Watenthedwa chifukwa cha Chikhristu

Mwana wina wa chipembedzo cha chikhristu mdziko la Pakistan waphedwa potenthedwa  ndi moto wa mafuta a Petulo atapezeka akuwuza anthu kuti iye ndi mkhristu. Malipoti ati mwanayu Noman Masih, anali wa...

View Article

Bungwe la ECM lakonza Mgonero Pofuna Kupeza Ndalama Zoyendetsera Kachebere...

Bungwe la ma episkopi mdziko muno la Episcopal Conference of Malawi ECM, kupyolera mu komiti yake yofufuza chuma choyendetsera sukulu yosulira ansembe ya Kachebere, lakonza mgonero pofuna kupeza...

View Article


Papa Franscisco Ayamikira ma Episkopi a Mdziko la Kenya.

Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wapempha ma episikopi a dziko la Kenya kuti adzipereke pautumiki wawo,pofuna kuti cholinga cha mpingowu pokhala chida chachiyanjano komanso...

View Article

Apolisi Mdziko la Italy Amanga Asilamu Khumi ndi Asanu.

Apolisi mdziko la Italy amanga anthu khumi ndi asanu a chisilamu omwe akuwaganizira kuti agwetsera akhristu khumi ndi awiri mmadzi pakusamvana komwe kunabuka m’boti lomwe anakwera paulendo opita ku...

View Article


Dimu Pamsewu

Ulaliki titled Dimu Pamsewu by Senia Kaunda

View Article

Nkhondo Ili Dzenjemu

Ulaliki titled Nkhondo ili  dzenjemu

View Article

Fanizo La Ana Awiri

Ulaliki titled Fanizo La Ana Awiri

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>