Anthu omwe Ali Paulendo waku Yerusalemu Apite ndi Cholinga Chimodzi
Akhristu omwe ali paulendo okamphera ku malo oyera ku Yerusalemu chaka chino awapempha kuti adzapite ku malowa ndi cholinga chimodzi chokapemphera kuti ayambe moyo watsopano. Mtsogoleri waulendowu...
View ArticleNtchito Yotolela Thandizo la Radio Maria Itha Lolemba
Ntchito yotolera thandizo la Radio Maria yotchedwa Mariatona yomwe imachitika m`masiku atatu ati itha lolemba pa 17 May 2015. Malinga ndi mkulu owona za maporogaramu ku wailesiyi Bambo Josephy Kimu...
View ArticleAmbuye Msusa Asankhidwa Kukhala Apostolic Administrator wa Dayosizi ya Zomba
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika padziko lonse Papa Francisco wasankha Olemekezeka Ambuye Thomas Luke Msusa,omwe ndi arkepiskopi wa arkdayosizi ya Blantyre kukhala woyendetsa dayosizi ya Zomba ngati...
View ArticleAnthu Pafupifupi 9 Sauzande Afa pa Ngozi ya Chivomerezi Mdziko la Nepal
Anthu oposa 8 sauzande 500 ndi omwe afa pangozi ziwiri za chivomerezi zomwe zagwedeza dziko la Nepal masiku apitawa. Malipoti a wailesi yakatolika ku likulu la mpingowu ku Vatican ati padakali pano...
View ArticleDziko la South Africa Labwenza Mzika za Mdziko la Mozambique Kwao
Dziko la South Africa labweza anthu oposa mazana anayi 400 a mdziko la Mozambique omwe amakhala mdzikolo alibe zitupa zowayenereza. Dzikolo lachita izi pambuyo pa ziwembu zomwe mzika za dzikolo...
View ArticleMalemu Sister Mzaza Ayikidwa Mmanda
Mwambo woyika mmanda thupi la malemu Sister Anastazia Mzaza a chipani cha Charity of Ottawa wachitika lolemba ku parish ya Ludzi m’boma la Mchinji. Sister Anastazia Mzaza,anabadwa pa 10 November mchaka...
View ArticleKusamvana Kukupitilira Mdziko La Burundi pa Chisankho chomwe Chichitike Mdzikolo
Boma la dziko la Burundi lati silibwenzera anthu omwe akukhudzidwa mugulu lomwe lakhazikitsidwa lofuna kuchotsa pampando Pulezidenti Pierre Nkuruzinza kuti asayimenso pa chisankho chomwe...
View ArticleBomba Lapha Anthu Asanu Ndi Awiri Mdziko La Nigeria.
Anthu asanu ndi awiri afa pa msika wina mdziko la Nigeria ndi bomba lomwe linaphulitsidwa pa msikawo. Malinga ndi malipoti a BBC aka ndi kachiwiri sabata ino izi kuchitika ku mpoto kwa dzikoli pomwenso...
View ArticleArk Episkopi Gabriel Anokye Wasankhidwa Kukhala Mkulu Wa Caritas...
Ark Episkopi wa mdziko la Ghana Gabriel Justice Yaw Anokye wasankhidwa kuti akhale mtsogoleri watsopano wa bungwe la Caritas International wa mmayiko a kuno Africa. Malinga ndi malipoti a wailesi ya...
View ArticleAsilikali a Mdziko la Nigeria Apulumutsa Amayi ndi Ana ku Zigawenga za Boko...
Dziko la Nigeria likusunga amayi ndi ana omwe apulumutsidwa mmanja mwa zigawenga za Boko Haram ku malo ena a asilikali pofuna kuti liziwasamalira mwanjira zosiyanasiyana. Kumalo a asilikaliwo,amayiwo...
View ArticleMutharika Atsekulira Chiwonetsero cha Malonda
Pulezidenti wadziko lino Proffesor Arthur Peter Mutharika wapempha a Malawi onse kuti agwirane manja pofuna kupititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino. Proffesor Mutharika wanena izi lachisanu pa...
View ArticleSister Stefani Akhazikitsidwa Kukhala Odala
Mwambo okhazikitsa malemu Sister Ireen Stefani kukhala odala wachitika loweruka lapitali mu ark dayosizi ya Nairobi mdziko la Kenya. Kadinala Polycarp Pengo yemwenso ndi arkepiskopi wa dayosizi ya Dar...
View ArticleSister Chikwawa a Chipani cha SBVM Amwalira
Sister Ellen Chikwawa a chipani asisteri cha Sisters of the Blessed Virgin Mary SBVM, amwalira. Sister Chikwawa,omwe amwalira la Mulungu madzulo, anabadwa mchaka cha 1940 mmudzi mwa Chimatila mdera la...
View ArticlePulezidenti Jonathan Akuyembekezeka Kutula Udindo Wake Lachisanu
Mtsogoleri wa dziko la Nigeria GoodLuck Jonathan,akuyembekezeka kupereka udindowu kwa mtsogoleri watsopano Muhamad Buhari lachisanu likudzali atalephera pachisankho cha pulezidenti chomwe chidachitika...
View ArticleNthambi ya CCJP ku Vatican Yati Chaka cha 2015 ndi Chofunika
Nthambi yowona za chilungamo ndi mtendere kulikulu la mpingo wakatolika ku Vatican lati chaka cha 2015 ndi chofunikira kwambiri pachitukuko cha mayiko. Mtsogoleri wa nthambiyi kulikululo Kadinala Peter...
View ArticleAkhristu akhale Olimba pa Chikhulupiliro Chawo Potsata Mphatso za Mzimu Woyera
Akhristu awapempha kuti akhale olimba pa chikhulupiliro chawo posiya makhalidwe omwe ndi osiyana ndi mphatso zomwe Mzimu Woyera umapereka . Nduna ya episkopi wa Arkidayosizi ya Blantyre Monsinyo...
View ArticleSister Chikwawa Ayikidwa Mmanda
Mwambo oyika m'manda thupi la malemu Sister Ellen Chikwawa wachitika lachiwiri ku likulu la chipani cha Atumiki a Maria Virgo ku Mary View ku Nguludi m'boma la Chiradzulu. Episkopi wa Dayosizi ya...
View ArticleMpingo wa Katolika Mdziko la Burundi ndi Wokhudzidwa
Mpingo wakatolika m’dziko la Burundi wati ndi wokhudzidwa ndi momwe zinthu zilili pa ntchito yokonzekera chisankho cha Pulezidenti chomwe dzikolo likuyembekezeka kukhala nacho mwezi wa mawa. Mpingowu...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Yakhazikitsa Ntchito Yothandiza Anthu omwe Anakhudzidwa...
Dayosizi ya Mangochi yakhadzikitsa ntchito yopereka thandizo kwa anthu amene anakhudzidwa ndi ngozi za kusefukira kwa madzi Mwambo wokhazikitsa ntchitoyi wachitikira pa msasa umene anthuwa akukhala...
View ArticleDziko la Burundi Lapempha Mzika zake Kupeleka Ndalama Zothandizira Chisankho
Dziko la Burundi lapempha mzika za dzikolo kuti zipereke ndalama zothandizira pa chisankho chomwe chikuyembekezeka kuchitika mdzikolo mwezi wa mawa. Izi zadza pomwe bungwe la mgwirizano wa maiko...
View Article