Makolo Atenge Udindo Wophunzitsa Ana Kulemekeza ma Alubino
Makolo mdziko muno awapempha kuti akhale ndi udindo ophunzitsa ana awo kulemekeza anthu amene ali ndi khungu la achi alubino. wachiwiri kwa wapampando wa bungwe la anthu a chi alubino mdziko muno la...
View ArticleKwaya ya St. Benadetta Masanjala, Nambala Wani mu Radio Maria Malawi Choir...
Kwaya ya St. Benadetakuchokera ku parishi ya Masanjala muarchdayosiziya Blantyrendi imene yatenga chikho cha chiphwando cha mayimbidwe (Choir Festival) cha Radio Maria Malawi ya chaka chino. Malinga...
View ArticleBambo Simon Nyalugwe Alowa M’manda
Mwambo woyika m’manda thupi la malemu bambo Simon Nyalugwe omwe amatumikira ku dayosizi ya mpingo wakatolika ya Zomba wachitika lolemba pa 22 August 2016ku Zomba Cathedral mu dayosizi ya Zomba. Malinga...
View ArticleMpingo Wakatolika Mdziko Muno ati Udzapindula ndi Msokhano wa WUCWO
Mpingo wakatolika mdziko muno akuti udzapindula kwambiri ndi msonkhano wa bungwe la amayi achikatolika pa dziko lonse waWorld Union of Catholic Women Organisation(WUCWO)umene awukonza kuti uchitikire...
View ArticleAmangidwa Kamba Kopezeka ndi 90 Kg ya Chamba
Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga mzika ziwiri za m’dziko la Zimbabwe ndi mzika ya dziko lino kamba kopezeka ndi chamba cholemera ma Kilogram 90. Malinga ndi othandizira ofesi ya zofalitsa nkhani za...
View ArticleECM Yapempha Nyumba Zofalitsa Nkhani Zachikatolika Kuti Zizilumikizana
Bungwe la ma episikopi a mpingo wakatolika m’dziko muno la Episcopal Conference of Malawi(ECM) lapempha nyumba zofalitsa nkhani za mpingo wakatolika kuti nthawi zonse pamene zikugwira ntchito zizigwira...
View ArticlePapa Francisko Apemphelera Mwapadera Anthu Okhudzidwa ndi Chiwembu Mdziko la...
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransiskolamulungu anachita mapemphero a padera opemphelera anthu onse omwe akhudzidwa ndi chiwembu cha mabomba chomwe chachitika ku m’mwera kwa...
View ArticlePapa Ayamikira Bungwe la ma Episkopi a Mdziko la Poland
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira bungwe la ma episkopi a mdziko la Poland kamba ka chisamaliro chabwino chomwe anamuwonetsera pa mwambo wa chaka cha achinyamata...
View ArticlePAC Ikuphunzitsa Amayi Luso Lobweretsa Mtendere
Bungwe la mgwilizano wa mipingo ndi zipembedzo laPublic Affairs Committee(PAC)lati likufuna kulimbikitsa kuphunzitsa amayi luso lothandiza kubweletsa mtendere pa nkhani zosiyanasiyana zochitika m’dziko...
View ArticlePapa Fransisko Wayamikiridwa ndi Chipembezo cha Chisilamu
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco amuyamikira kamba kothilirapo ndemanga ponena kuti chipembedzo cha chisilamu si chofanana ndi magulu omwe amakhala akuchita za uchifwamba....
View ArticleKunkuyu Wakhazikitsa Chipani cha Transformation Alliance
Nduna yakale ya zofalitsa nkhani mu ulamuliro wa Dr. Joyce Banda a Moses Kumkuyu achita mwambo wokhadzikitsa chipani chawo cha ndale. Poyankhula pokhazikitsa chipanichi chomwe akuchitchula kuti...
View ArticleMpingo Ulimbikitsa Mabanja Kukhala Olimba, Okhazikika mu Chikhristu
Mpingo wakatolika m’dziko muno wati udzipereka polimbikitsa mabanja opezeka mu mpingo-wu kukhala olimba ndi okhazikika pa chikhristu chawo. Mkulu wa kuofesi yoona za mabungwe a utumiki wa a Papa ku...
View ArticleDeath Announcement
The Diocese of Mangochi regrets to announce the death of FR. BARTHOLOMEW PHWERUWA of Mangochi Diocese. Fr. Phweruwa has passed on today, 28th August 2016 at Mlambe Hospital in Blantyre. Brief History...
View ArticleAngoni Opezeka Ku Blantyre Apempha Anthu Athandize Pothetsa Mavuto pa...
Bungwe la Angoni omwe akupezeka mu mzinda wa Blantyre la Maseko Ngoni Blantyre Chapter lapempha anthu kuti agwirane nawo manja pothandizapo pa mavuto omwe odwala a pachipatala cha Ntcheu amakumana...
View ArticleMabungwe Agwiritse Ntchito Radio Maria Malawi Ngati Chida Chofalitsira...
Bungwe la Legio Ya Maria lochokera ku Kachebere mu arkidayosizi ya Lilongwe lapempha mabungwe osiyanasiyana mu mpingo wa katolika kuti azigwiritsa ntchito Radio Maria Malawi ngati chida chofalitsira...
View ArticleAkhristu Azilowa Bungwe la Awerengi
Akhristu a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti azikonda kulowa bungwe la awerengi chifukwa ndi bungwe lomwe limazama kwambiri pa kuwerenga mawu a Mulungu. Wapampando wa bungwe la awerengi pa...
View ArticleJacobs Mwase 'Zakaliya' Wamwalira
M'modzi mwa akatswiri a zisudzo mdziko muno Jacobs Mwase amene amatchukandi dzina loti a Zakaliya wamwalira. M'modzi mwa akuluakulu omwe amachita zisudzo mugulu la Kwathu Drama, a Eric Mabedi...
View ArticleM’modzi mwa Akuluakulu a Islamic State (IS) Waphedwa
M’modzi mwa akuluakulu a gulu la zauchifwamba la Islamic State (IS)a Abu Muhammad Al-Adnani ati waphedwa m’dziko la Syria. Mkuluyi ati ndi yemwe anachititsa kuti anthu ambiri a mchigawo cha kumvuma kwa...
View ArticleKusakwanira kwa Mauthenga a Apolisi Kukukolezera Mchitidwe Ophana ku Nkhatabay
Kusakwanira kwa mauthenga a apolisi pa kayendetsedwe ka milandu akuti kukukolezera kukula kwa mchitidwe ophana komanso kuzipha m’boma la Nkhatabay. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali, Sergeant...
View ArticleGalimoto Lapha M’modzi ndi Kuvulaza Atatu M’boma la Mangochi
Galimoto lina lomwe woyendetsa wake sakudziwika ati lapha m’nyamata wa zaka khumi ndi zinayi (14) ndi kuvulaza ena atatu m’boma la Mangochi. Malinga ndi wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi m’boma...
View Article