Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Papa Wapepesa Dziko la Mexico, America

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wapereka  uthenga wachipepeso kwa anthu omwe akhuzidwa ndi mphepo ya mphamvu yomwe yakhuza anthu a m’maiko a Mexico komanso America....

View Article


Afa Atatsamwidwa ndi Chingamu

M`nyamata wina wa zaka zisanu ndi ziwiri (7) wafa atatsamwidwa ndi chingamu ku Bangwe munzinda wa Blantyre. Malinga ndiwothandizira mu ofesi yazofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe, Sergent Widson...

View Article


Bambo Albert Chandiyang`ana Alowa M’manda

Mwambo woika m`manda thupi la Bambo Albert Chandiyang`ana  amu arkidayosizi ya Blantyrewachitika lachinayi ku ku St. Louis Montfort CI Parish  mu arkidayosiziyo. Mwambowu unayamba ndi msembe ya...

View Article

Anthu 7 Afa Pa Ngozi Ku Ntcheu

Anthu asanu ndi awiri 7 afa ndipo ena avulala  basi yomwe anakwera itagwa  pa Mlangeni  m`boma la Ntcheu. Wofalitsa nkhani za apolisi m`bomali a Gift Matewere atsimikiza zankhaniyi  ndipo ati basiyi...

View Article

COOPI Ikulimbikitsa Kudzidalira Kwa Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zogwa...

Bungwe la Cooperazione Internazionale (COOPI) lati liwonetsetsa kuti likupititsa patsogolo kudzidalira kwa anthu amene akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi mdziko muno. Wamkulu wa bungweli mdziko...

View Article


Ofalitsa Nkhani Aboma Awalangiza Kuphunzitsa Anthu Zandondomeko za Ntchito za...

Anthu ogwira ntchito  m`maofesi ofalitsa nkhani  aboma  ochokera m`maboma osiyanasiyana awalangiza  kuti  akhale patsogolo kuphunzitsa anthu zandondomeko  za ntchito za boma. Nduna yazofalitsa nkhani...

View Article

Mpingo Wakatolika Upitiriza Kufalitsa Uthenga, Kuthandiza Boma Kudzera Mu...

Mpingo wa katolika m’dziko muno wati kudzera mu chipani cha mofolo woyera upitiriza kufalitsa uthenga wa Mulungu ponseponse ndi cholinga chokuti akhristu ake azame mu chikhristu chawo. Episkopi wa...

View Article

Dziko la Nigeria Lalengeza Kuti Lichita Kampeni Yopereka Katemera Wa Matenda...

Dziko laNigeria lalengeza kuti lichita kampeni yopereka katemera wothana ndi matenda a Polio, potsatira kubukanso kwa matendawa m`dzikolo. Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC,   ana awiri alumala...

View Article


Papa Ayendera Amayi 20 Omwe Anazembetsedwa M’maiko Awo

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonsePapa Francisco wayendera amayi makumi awiri (20) omwe anabedwa ndi kuzembetsedwa kuchokera ku maiko awo ndikukagulitsidwa ku maiko ena cholinga choti...

View Article


Boko Haram Yatulutsa Kanema Yowonetsa Atsikana Omwe Ikusunga

Gulu la za uchifwamba mdziko la Nigeria la Boko Haram latulutsa kanema yowonetsa ena mwa atsikana omwe gululi linagwira mdera la Chibok ndipo likuwasunga. Malinga ndi malipoti a wasilesi ya BBC,...

View Article

Bungwe la SCORE_ECD Lati Lipitiriza Kusula Alezi a Sukulu za Mkombaphala

Bungwe la Strengthen Capacity of Religious Women In Early Childhood Development (SCORE-ECD) lati lipitiriza kusula alezi a msukulu za mkombaphala za chikatolika mdziko muno ndi cholinga chopititsa...

View Article

Boma Liyamba Kugawa Chakudya Posachedwapa

Boma lati liyamba kugawa chakudya posasedwapa m’maboma onse omwe akhudzidwa ndi vuto la njala m’dziko muno. Nduna ya zofalitsa nkhani ndi kuphunzitsa anthu wolemekezeka mayi Patricia Kaliati anena izi...

View Article

Amalawi Agwirane Manja Potukula Ntchito Zaumoyo

Anthu m`dziko muno awapempha kuti agwirane manja ndi boma polimbikitsa ntchito za umoyo. Mkulu wa bungwe lothandiza anthu osowa la Chisomo Support for The Needy a Mcsayitings Mdoka alankhula izi mu...

View Article


Anthu 30 afa Pachiwembu Mdziko la DRC

Anthu makumi atatu (30),afa gulu la zauchifwamba litachitira chiwembu mudzi wina m`dziko la  Democratic Replican of Congo (DRC). Guluri ati linachitira chiwembu mudzi  Rwagomaomwe uli pafupi ndi tawuni...

View Article

Canon Chizito a Mpingo wa Anglican Amwalira

Dayosizi ya Upper Shire ya mpingo wa Anglican yalengeza za imfa ya wansembe wopuma wa mpingowu Canon Arthur Chizito. Malinga ndi chikalata chomwe akulikulu la dayosiziyi atulutsa Canon Chizito amwalira...

View Article


Patel Apempha Mabungwe Ayambiretu Kulimbikitsa 50-50 Campaign

Boma komanso mabungwe omwe amalimbikitsa kuti pasakhale kusiyana pakati pa amuna komanso akazi awapempha kuti ayambe pano kulimbikitsa kampeni yomema anthu kuti avotere amayi ku nyumba ya malamulo ya...

View Article

Arkibishop Msusa Apempha Akhristu Akhale Ogwirizana Monga Apostoli

Akhristu a mpingo wa katolika awapempha kuti akhale ogwirizana monga m`mene apostoli oyamba aja ankachitira atalandira mphamvu za mzimu oyera. Arkepiscopi wa archdayosizi ya Blantyre wolemekezeka...

View Article


Papa ndi Okhudzidwa ndi Imfa ya Anthu Anayi Mdziko la Portugal

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco wati ndi wokhudzidwa ndi imfa ya anthu anayi omwe afa kamba ka ngozi ya moto wachilengedwe umene unabuka mu nkhalango ina m’dziko la...

View Article

CADECOM Yapempa Atolankhani Kuti Alimbike Pothana Ndi Matenda A Kunyentchera

Nthambi yoona za chitukuko mu mpingo wa katolika ya Catholic Development Committee (CADECOM) mu dayosizi ya Zomba yati atolankhani ali ndi udindo waukulu ophunzitsa anthu kuyipa kwa matenda...

View Article

Aphunzitsi Achikatolika M’boma La Zomba Awayamikira Kamba Kothandiza Odwala

Aphunzitsi abungwe la chikatolika ku parish ya Mayaka  m’boma la Zomba awayamikira chifukwa cha chidwi chawo chofuna kuthandiza odwala. Mmodzi mwa akulu akulu pa chipatala cha chikulu cha Zomba Mayi...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>