Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Bomba Lapha Anthu Khumi Mdziko la Pakistan

Anthu khumi afa ndipo ena makumi atatu avulala potsatira bomba lomwe linaponyedwa pa bwalo lina lozengera milandu mu mzinda wa Mardan kumpoto kwa dziko la Pakistan. Malipoti a wailesi ya BBC ati munthu...

View Article


Otsutsa Achita Chionetsero Pofuna Kuchotsa President Maduro Pampando

Anthu otsutsa boma zikwizikwi mu mzinda wa Caracasm’dziko la Venezuela ati anachita zionetsero pofuna kuti mtsogoleri wa dzikolo Nicholas Maduro achotsedwe pa udindo wake. Malinga ndi malipoti a...

View Article


ZARDD Ikuchepetsa Njala ku Chingale Kudzera mu Ulimi Wamthilira

Anthu a m’dera la Chingale m’boma la Zomba ati ndi okhutira ndi ntchito zomwe nthambi ya chitukuko ya dayosizi ya Zomba ya Zomba Diocese Research and Development (ZARDD) ikugwira m’derali pothandiza...

View Article

CIM Yakhazikitsa Magazine Ya Za Malonda Ya Ulere

Bungwe la mgwirizano wa anthu owona za malonda mdziko muno la Chartered Institute of Marketing-CIM lakhazikitsa magazine yomwe iziperekedwa mwa ulere ndipo cholinga chake ndikufuna kupititsa patsogolo...

View Article

SAFE lkuthandiza Boma Potukula Maphunziro

Bungwe lomwe silaboma laSub Sahara African Enrichment (SAFE)lati lipitiliza kuthandiza boma potukula maphunziro m’dziko muno. Mkulu wa bungweli Professor Moira Chimombo walankhula izi pa maphunziro...

View Article


Papa Francisco Alimbikitsa Ansembe Kuthandiza Akhristu pa Mavuto

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisco walimbikitsa ansembe mu mpingowu kuti azikhala okhudzidwa ndi kuthandiza pa mavuto omwe akhristu akukumana nawo. Papa wati ansembe...

View Article

Dziko la Germany Litseka Zipata Zake ndi Dziko la Australia

Dziko la Germany lati litseka zina mwa zipata zake ndi dziko la Australia pofuna kuchepetsa anthu othawa kwawo omwe akulowa m`dzikolo kudzera mdziko la Australia lo. Akuluakulu a dziko la Germany ati...

View Article

Dziko la China Lamanga Episkopi Wodzalowa M’malo Mwa Bishop Wopuma

Akuluakulu a dziko la China ati amanga episkopi wodzalowa m’malo mwa bishop wopuma wa mpingo wakatolika ndi kumuchotsa ku dayosizi yomwe amatumikira pofuna kuti asakhazikitsidwe kukhala episkopi...

View Article


Alimi Apindula Ndi Mbewu za Mtundu wa Nyemba Chaka Chino

Boma lati alimi mdziko muno apindura kwambiri ndi zokolola zawo posatira mgwirizano omwe lachita ndi dziko la India lomwe lawonetsa chidwi chogula mbewu za mtundu wa nyemba Nduna ya za ulimi ulimi wa...

View Article


Akhristu Agwire Ntchito Zachifundo, Mapemphero Muchaka cha Chifundo cha Mulungu

Akhristu m’dziko muno awapempha kuti ayesetse kuchita ntchito za chifundo komanso kuchulutsa mapemphero chaka cha jubili ya chifundo cha Mulungu chisanafike kumapeto. Katikisiti Patrick Kaligomba wa...

View Article

Papa Wapepesa Dziko la Romania Kamba ka Ngozi ya Moto

Mtsogoleri wa Mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapepesa Pulezident wa dziko la Romania potsatira ngozi ya moto yomwe yapha anthu makumi atatu ndi awiri, ndikuvulaza ena 130 mu m’dzinda...

View Article

Mbava Zaba ku Nyumba ya Ansembe ku Parishi ya Neno

Akuba okhala ndi zikwanje ati avulaza modetsa nkhawa alonda awiri ndi kuba katundu osiyanasiyana ku nyumba ya ansembe pa parishi ya mpingo wakatolika ya Neno mu archdayosizi ya Blantyre. Bambo mfumu a...

View Article

Nthambi ya Radio Maria Malawi ya Lilongwe Ikufuna Thandizo Logulira Zida

Achinyamata omwe amatumikira ku nthambi ya Radio Maria Malawi ya ku Lilongwe ati amazindikira bwino kuti ntchito yawo ndi yofuna kukweza dzina la Amai Maria komanso kuthandiza ena kumvetsetsa mawu a...

View Article


Papa Apemphelera Dziko la Gabon

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco anachita mapemphero apadera opemphelera dziko la Gabon potsatira zamtopola zomwe zipani za ndale zikuchita mdzikolo. Polankhula pa mwambo...

View Article

Episkopi Apempha Akhristu Apite ku Malo Oyera Chaka cha Chifundo Chisanathe

Episkopi wa dayosizi ya mpingo wakatolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima apempha akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno kuti chaka cha jubilee ya chifundo cha Mulungu chisanathe apite ku malo...

View Article


Chilima Apempha Akhristu Agule New Catholic Answer Bible

Akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno awapempha kuti agule baibulo la tsopano la mpingowu lomwe akulitcha New Catholic Answer Bible ndi cholinga choti azame mu chikhulupiliro chawo komanso...

View Article

JOINT MEDIA AND ADVOCACY STATEMENT

1.0. PREAMBLE The Catholic Commission for Justice and Peace (CCJP) which is a social justice and advocacy arm; and the Research and Social Commission which is the communication arm of the Episcopal...

View Article


Proud Catholic Mangochi

Proud catholics in the Diocese of Mangochi cheered prisoners at Mangochi prison today 17th September 2016. It was wonderful charity activity. By the grace of God they managed to share to each of them a...

View Article

Anthu Atatu Afa pa Ngozi ya pa Shoprite

Chiwerengero cha anthu omwe afa pa ngozi yomwe yachitikadzulopa Shoprite mu msewu wa Masauko-Chipembere mu mzinda wa Blantyreakuti chafika pa atatu. Ngoziyi yachitika dzuro cha ku m’mawa, galimoto la...

View Article

Pope thanks Vatican Security

Pope Francis on Sunday thanked the Vatican security force for their tireless service and warned against crimes that are connected to exploitation and corruption. The Pope’s words came as he celebrated...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>