Papa Apepesa Okhudzidwa pa Ngozi ya Ndege Mdziko la Hong-Kong
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonsePapa Franciscowapereka uthenga wa chipepeso kwa anthu amene akhudzidwa pa ngozi ya ndege yomwe yagwa mu mzinda waKyrgyzstanmdziko laHong-Kong. Malipoti a...
View ArticleNtchito Yofufuza MH370 Yaimitsidwa
Ntchito yofufuza ndege ya MH370 ya mdziko la Malaysia yomwe inasowa zaka zitatu zapitazo ati ayamba ayiyimitsa. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, mayiko a Australia, Malaysia komanso China aganiza...
View ArticleApempha Anthu Apitirize Kugwirana Manja ndi Apolisi
Anthu okhala mdera la mfumu yayikulu Bvumbwe m’boma la Thyolo awapempha kuti apitirize kugwirana manja ndi apolisi pa ntchito yolimbikitsa chitetezo cha ku madera. Mkulu wa apolisi ya m’delari a...
View ArticlePapa Wati Ndi Udindo Wa Aliyense Kusamalira Ndi Kuteteza Ana
M'tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisko wati ndi udindo wa munthu aliyense kuwonenetsetsa kuti ana akulandira chisamaliro ndi chitetezo chabwino. Papa walankhula izi lachitatu...
View ArticleAsilikali Apulumutsa Ana 53 Omwe Anabedwa Ku Ethiopia
Asilikali m’dziko la Ethiopia ati akwananitsa kupulumutsa ana makumi asanu ndi atatu 53 omwe anabedwa ndi gulu lina la zigawenga m’dzikomo. Malingana ndi malipoti a wailesi ya BBC anawa akuti anagwidwa...
View ArticleJammeh Watuluka Mdziko la Gambia
Mtsogoleri wakale wa dziko la Gambia, Yahya Jammeh wachoka mdzikolo atavomereza kugonja kwake pa chisankho atalamulira dzikolo kwa zaka 22. Malipoti a wailesi ya BBC ati Jammeh pakadali pano ali mdziko...
View ArticlePapa Apempha Akhristu Alimbikitse Umodzi, Apemphelera Okhudzidwa Ndi Zivomerezi
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha akhristu kuti agwirane manja popemphelera umodzi pakati pawo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya Vatican ati papa wanena izi...
View ArticleRadio Maria Malawi Yakonzeka Kutumikira Omvera Ake Mchaka Cha 2017
Radio Maria Malawiati yakonza ndondomeko zosiyanasiyana pofuna kupititsa patsogolo ntchito za wailesiyi ndi cholinga choti itumikire bwino omvera ake mchaka cha 2017. Mkulu woyendetsa mapologalamuku...
View ArticleAnthu 18 Afa Kamba ka Nyengo Yoipa Mdziko la America
Anthu pafupifupi 18 afa ndipo ena ambiri avulala kutsatira nyengo yoipa kum’mwera kwa dziko la America. Malipoti a wailesi ya BBC ati gavanala wa ku Georgia walengeza kuti madera asanu ndi awiri 7...
View Article11 Million Dollars Zasowa Mdziko la Gambia
Ndalama zoposa 11 million za America akuti zasowa mdziko la Gambia kutsatira kuchoka kwa mtsogoleri wa kale wa dzikolo a Yahya Jammeh. Malipoti a wailesi ya BBC ati pali chisonyezo chakuti a Jammeh aba...
View ArticleBungwe la CCJP Lati Ntchito ya Chilungamo cha Mmudzi Ikupindulira Anthu
Bungwe la chilungamo ndi mtendere CCJP mu Arch dayosizi ya Blantyre ya mpingo wakatolika lati ndi lokhutira ndi momwe ntchito yothandiza anthu kumvetsa ma ufulu awo ndi kupereka uphungu pa milandu...
View ArticlePapa wati Mauthenga Azibweretsa Kusintha
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco walimbikitsa anthu kuti akhale ndi kuthekera kwabwino kopereka mauthenga ndi cholinga chofuna kuti dziko lonse liziyenda mu chowona komanso...
View ArticleMaepiskopi a Mdziko la America Sakugwirizana ndi Maganizo a Trump
Maepiskopi a Mdziko la America Sakugwirizana ndi Maganizo a Trump Bungwe la maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la America la United States Conference of Catholic Bishops latsutsa maganizo a...
View ArticleMipingo ya M’dera la Chimwala Ichita Mwambo wa Umodzi wa Akhristu
Mipingo ya chikhristu yopezeka m’dera la aSenior Chief Chimwalam’boma laMangochiayiyamikira kamba kodzipeleka pa ntchito zolimbikitsa umodzi pakati pawo. Mkulu woyendetsa ntchito za umodzi wa mipingo...
View ArticleDziko la Columbia Likufuna Kuthetsa Kulima Mbewu ya Coca
Dziko la Columbia lalengeza za mapulani ofuna kuthetsa kulima mbewu ya Coca yomwe amapangira mankhwala ozunguza bongo a Cocaine. Malipoti a wailesi ya BBC ati alimi amene achotse mbewu zawo okha...
View ArticleTrump Aletsa Mzika za Syria Kulowa Mdziko la America
Mtsogoleri wa dziko la America, Donald Trump wayimitsa ndondomeko ya anthu othawa kwawo ya dzikolo ndipo waletsa anthu a mdziko la Syria kulowa mdziko la America. Malipoti a wailesi ya BBC ati...
View ArticlePapa Apereka Uthenga wa Chipepeso ku Dziko la Chile
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ati wapereka uthenga wa chipepeso kwa anthu onse omwe ataya abale awo komanso omwe akhudzidwa pa ngozi ya moto wachilengedwe mchigawo...
View ArticlePapa Ayamikira Ziwonetsero Zoteteza Moyo Mdziko La America
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira onse omwe anatenga nawo mbali pa ulendo wa ndawala woteteza ufulu wa moyo womwe wachitika dzulo lachisanu mu mzinda wa...
View ArticleCADECOM Iwonetsetsa Kuti Anthu Akukhala ndi Chakudya Chokwanira
Bungwe la CADECOM mu dayosizi ya Zombalati liwonetsetsa kuti anthu mu dayosiziyo akukhala ndi chakudya chokwanira ngakhale nyengo ikusintha. Mkulu wa bungwe la CADECOM mu dayosizi yo bambo Patrick...
View ArticleDr. Kumpalume Achenjeza Anthu Ochita Chinyengo Mzipatala za Boma
Unduna wa zaumoyo wati uthana ndi anthu onse ochita zachinyengo mu ntchito ya zaumoyo mdziko muno. Nduna mu undunawu Dr. Peter Kumpalume ndi omwe anena izi pa mwambo omwe bungwe la Clinton Health...
View Article