Kaliati Wayamikira Mpingo Wakatolika Podzipereka Kufalitsa Uthenga Wabwino
Mpingo wakatolika m’dziko muno awuyamikira kamba kodzipereka pa ntchito zofalitsa uthenga wabwino. Nduna ya zofalitsa nkhani ndi kuphunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana mayiPatricia Kaliati ndi omwe...
View ArticleNtchito Yolumikiza Magetsi Mmidzi Idya 8 Billion Kwacha
Boma lati ntchito yolumikiza magetsi m’madera akumidzi ikuyembekezeka kudya ndalama zokwana 8 Billion kwacha. Nduna yoona za chilengedwe komanso mphamvu za magetsi a Bright Nsaka ati gawoli ndi la...
View ArticleMphamvu za Mpingo Wakatolika Zili pa Akhristu Ovutika Mchikhulupiliro-Papa
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wati mphamvu za mpingo wa Katolika zatsamira kwambiri pa akhristu ochepa omwe akuvutikabe kaamba ka chikhulupiliro chawo. Iye amalankhula...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Ilimbikitsa Achinyamata Kutenga Mbali mu Mpingo
Dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi yati iwonetsetsa kuti achinyamata akutenga nawo mbali pa zochitika zonse za mpingo. Mlembi wa episkopi wa dayosiziyi bambo Steven Kamanga anena izi pa...
View ArticleDziko La Indonesia Lidzudzula President Trump
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Indonesia a Jusuf Kalla wati ndondomeko yomwe dziko la America lokonza poletsa anthu ochokera ku Mayiko a chisilamu kulowa mdziko la America, kukupereka chikayiko...
View ArticleTrump wati Sakudana ndi Chipembedzo cha Chisilamu
Mtsogoleri wa dziko la America Donald Trump wati ganizo lake loletsa nzika zina zochokera ku mayiko ena achisilamu kulowa mdzikolo sikukutanthauza kuti akudana ndi chipembedzo chachisilamu. A Trump...
View ArticlePapa wati Chipulumutso Chikuyenera Kuvalidwa Ngati Chipewa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti avale chiyembekezo cha chipulumutso ngati chipewa chodzitetezera pa ngozi ya njinga pozindikira kuti kuwuka kwa...
View ArticleMamuna Wina Wamira M’boma la Ntchisi
Mamuna wina m’boma la Ntchisi ati wafa atamira mu mtsinje wa Bua komwe anapita kukawedza nsomba. Wofalitsa nkhani za apolisi mbomali Sergent Gladson M’bumpha watsimikiza za nkhaniyi. Sergent M’bumpha...
View ArticlePapa Francisko Wakhazikitsa Stanislaus ndi Maria Elizabeti Kukhala Oyera
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisko wakhazikitsa Stanislaus wa Yosefe ndi Maria komanso Maria Elizabeti Hesselblad kukhala oyera. Papa wakhazikitsa awiriwa kukhala oyera...
View ArticleAnthu Asanu Ochita Masewero Opalasa Njinga Afa Atagundidwa Ndi Galimoto
Anthu asanu ochita masewero opalasa njinga afa ndipo ena anayi avulala galimoto lina litawaomba ku Michigan m’dziko la America. Anthu-wa ati agundidwa ndi galimoto la mtundu wa Pick Up lomwe pa...
View ArticlePapa Apempha Akhristu Azipemphelera Atumiki a Mulungu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu kuti azipemphelera atumiki a Mulungu omwe anayitanidwa kuti atumikire Mulungu. Papa amalankhula izi ku likulu la mpingowu ku...
View ArticleAmbuye Msusa Adandaula Kamba ka Kusagwiritsa Ntchito Bwino Chilengedwe
Arkiepiskopi wa arkidayosizi ya Blantyre ya mpingo wakatolika Ambuye Thomas Luke Msusa wadandaula kuti dziko la Malawi likulephera kugwiritsa ntchito moyenera zachilengedwe zomwe lili nazo. Ambuye...
View ArticleMsilikali Amangidwa Kamba Kobera Anthu Ndalama
Apolisi m’boma la Karonga ati akusunga mchitokosi msilikali wina wa ku Cobbe barracks ku Zomba kaamba komuganizira kuti amalandira ndalama zokwana 80 sauzande kwacha kwa anthu a mmidzi ina ya m’bomalo...
View ArticleApolisi M’dziko la New Guinea Akuwaganizira Kuti Apha Ophunzira Anayi Omwe...
Apolisi m’dziko la New Guinea akuwaganizira kuti apha ophunzira anayi a pa sukulu ina ya ukachenjede omwe amachita chionetsero chosonyeza kusakondwa ndi zochita za nduna yaikulu ya dzikolo. Malingana...
View ArticleAnthu Makumi Atatu Afa Zigawenga za Islamic State Zitaphulitsa Bomba La Timke...
Anthu makumi atatu afa, ndipo ena 80 avulala gulu la zigawenga la Islamic State litaphulitsa mabomba awiri atinkenawo munzinda wa Baghdad m`dziko la Iraq Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, bomba...
View ArticleAnthu Asanu Ochita Masewero Opalasa Njinga Afa Atagundidwa Ndi Galimoto
Anthu asanu ochita masewero opalasa njinga afa ndipo ena anayi avulala galimoto lina litawaomba ku Michigan m’dziko la America. Anthu-wa ati agundidwa ndi galimoto la mtundu wa Pick Up lomwe pa...
View ArticlePapa Wati Akhristu Apempherere Mtendere wa Mmaiko Onse
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Franciskowapempha anthu ndi akhristu a mpingowu kuti lachitatu akumbukire kupemphelera mtendere wa m’mayiko pa dziko lonse. Malinga ndi malipoti a...
View ArticleNthambi Ya Zachilungamo Igwirizana Ndi Lamulo La Trump
Nthambi ya zachilungamo mdziko la America yati ikugwirizana ndi zomwe mtsogoleri wa dzikolo, Donald Trump wachita poletsa anthu a m’maiko ena a chisilamu kolowa mdzikolo. Malinga ndi malipoti a...
View ArticleMayi Afa pa Ngozi ya pa Nsewu M’boma la Mangochi
Mayi wina wa zaka 52 zakubadwa wafa atawombedwa ndi galimoto m’boma la Mangochi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergeant Amina Tepani Daudi wauza Radio Maria Malawi kuti mayiyu Martha Kuswenje...
View ArticleKanyongolo Wapempha Boma Libwezeretse Maubale Ndi Maiko Ena
Katswiri wa malamulo yemwenso ndi mphunzitsi wa malamulo pa sukulu ya ukachenjende ya Chancellor, Professor Edge Kanyongolo wapempha boma kuti libwezeretse ubale womwe unasokonekera pakati pa boma la...
View Article