Apolisi Mdziko la Turkey Amanga Anthu Omwe Akukhudzidwa ndi Chiwembu Cha...
Apolisi mdziko la Turkey ati amanga anthu angapo omwe akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi chiwembu chomwe chinaphetsa anthu 39 pa malo ena achisangalalo mdzikolo. Malipoti a wailesi ya BBCati anthu...
View ArticleApempha Makhansala Azibweretsa Zitukuko M’ma Ward Mwawo
Makhansala mdziko muno awapempha kuti azigwira ntchito yobweretsa chitukuko m’ma ward mwawo kuti anthu amene anawasankha aziwakhulupilira. Khansala wa ward ya Sadzi mu mzinda wa Zomba mayi Mercy...
View ArticlePapa ndi Wokhudzidwa ndi za Mtopola za Mdziko la Brazil
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndi okhudzidwa ndi zamtopola zomwe zachitika pa ndende ina zomwe zaphetsa anthu oposera makumi asanu 50 mdziko la Brazil. Papa...
View ArticleNdege ina ya mdziko la Egypt Yasowa
Ndege ina ya mdziko la Egypt yomwe imachokera mu mzinda wa Paris kupita mu mzinda wa Cairo ati yasowa mu mlengalenga itanyamula anthu okwana 66. Malinga ndi malipoti ndegeyo ati yasowa kuzambwe kwa...
View ArticlePulezidenti Wopuma wa Dziko la Iran Wamwalira
Mtsogoleri wa dziko la Iran a Ayatollah Ali watsogolera anthu mdzikolo kukhudza imfa ya mtsogoleri wopuma wa dzikolo a Akbar Hashem Rafsanjani omwe amwalira ali ndi zaka 82. Malinga ndi malipoti a...
View ArticlePapa Apereka Sakramenti la Ubatizo Kwa Ana 28
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wapereka sacrament la ubatizo kwa ana okwana 28 pa nsembe ya misa yomwe inachitikira mu tchalitchi la Sistine. Malinga ndi malipoti a...
View ArticleApolisi Ayamikira Mgwirizano ndi Anthu a Kumudzi
Mkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mawa kwa dziko lino Commissioner Effie Kaitano wathokoza mafumu, anthu akumudzi komanso apolisi eni ake kaamba kogwirana manja pa ntchito yochepetsa umbava ndi...
View ArticleObama Apempha Anthu Ateteze Ufulu Wa Democracy
Mtsogoleri wopuma wa dziko la America, Barrack Obama wapempha anthu m’dzikolo kuti akhale oteteza ufulu wa dimokalase. Malipotia wailesi yaBBCatiObamaamalankhula izi mu mzinda wa Chicago kudzera mu...
View ArticleEngineer Wazipha Pozimangilira
Bambo wina yemwe amagwira ntchito ngati engineer ku bwalo la ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe wazipha pozimangilira ku denga la nyumba yake. Malinga ndi wofalitsa nkhani za polisi pa bwalo la...
View ArticleDr. Chaponda Alamulidwa Kuti Ayime Kaye pa Unduna
Bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Mzuzu lagamula kuti nduna ya za ulimi chitukuko cha madzi ndi nthilira Dr. George Chaponda ayime kaye pa udindowu kufikira zofufuza zokhudza chimanga chomwe boma...
View ArticleAmangidwa Kamba Kopezeka ndi Mankhwala Popanda Chilolezo
Apolisi m’boma la Mangochi akusunga mchitokosi amuna awiri kaamba kopezeka ndi mankhwala popanda chilolezo. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Amina Tepani Daudiwati apolisi...
View ArticleChipatala Cha Kalembo Chikusowa Malo
Chipatala cha Kalembo m'boma la Balaka ati chikusowa malo owonjezelera chipatachi kaamba koti anthu ena analowelera malo a chipatalachi. Dotolo wamkulu pa chipatalachi Patricia Tembo wauza Radio Maria...
View ArticleKazembe wa Dziko la Australia Ayamikira Papa Francisco
Kazembe wa dziko la Australia wayamikira mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco kaamba ka mawu a mphamvu okhudza kudzetsa mtendere komanso kuteteza anthu othawa kwawo. Malipoti...
View ArticleApempha Akhristu Athandize Seminale Ya St. Peters
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awapempha akuti adzipeleke pa ntchito yosamalira seminale yayikulu ya St. Peters yomwe ili mu Dayosizi ya Zomba. Mkulu woyendetsa ntchito za seminalyi bambo...
View ArticleMOAM Yakhumudwa Ndi Anthu Okwera Minibus
Bungwe la eni minibus m’dziko muno laMinibus Owners Association of Malawi (MOAM) lati ndilokhumudwa kuti anthu okwera ndi amene akuthandizira kuti ma minibus m’dziko muno azinyamula anthu mopyola...
View ArticleTaliban Yatulutsa Kanema Wa Amuna Awiri Amene Akuwasunga
Gulu la za uchifwamba la Taliban ati latulutsa kanema amene akuwonetsa amuna awiri omwe zigawengazi zinawaba ndipo zikuwasunga mokakamiza. Malipoti a wailesi ya BBC ati Kelvin King wa mdziko la America...
View ArticleBambo Hernandez Apezeka Atafa
Wansembe yemwe anasowa masiku apitawa mdziko la Mexico akuti wapezeka atafa mdera lina lotchedwa Parras mdzikolo. Malinga ndi malipoti a CNA wansembeyu Joaqui’n Hernandez yemwe amatumikira mu dayosizi...
View ArticlePapa Francisco Akumana ndi Mtsogoleri wa Dziko la Palestine
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Fransiscoanakomana ndi mtsogoleri wa dziko la Palestine ku Vatican pa ulendo wake wokakomana ndi nduna yaikulu ya mdziko la Italy. Malinga ndi...
View ArticleArkidayosizi ya Lilongwe Ilimbikitsa Ana Kusamalira Chilengedwe
Mpingo wakatolika mu arch-dayosizi ya Lilongwe walimbikitsa ana mu mpingo-wu kuti apitirize kudzipereka pa nkhani zakusamilira chilengedwe pofuna kuthana ndi mavuto omwe akudza kaamba kakusintha kwa...
View ArticleWapolisi Afa Atamwa Mankhwala a Kwa Sing’anga
Wapolisi m’boma laNkhatabay wafa atamwa mankhwala azitsamba omwe sing’anga wina anamupatsa kuti achire ku matenda a m’mimba omwe amadwala. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomaloSergeantIgnasio...
View Article