Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Papa Atsekulira Malo Ochapira a Ulere

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisco watsegulira malo omwe anthu ovutika  azikagwilitsa ntchito akafuna kuchapa komanso kusitilako zovala mwa ulele mu mzinda wa Vatican mdziko...

View Article


Bambo Apha Anthu Atatu Mdziko la America

Anthu atatu afa ataomberedwa ndi bambo wina pa sukulu ina yomwe ili kumpoto kwa dera la San Bernardino mu mzinda wa Califonia mdziko la America. Malipoti a wailesi ya BBC ati munthuyu anaombera...

View Article


UN Yapempha Bata Mdziko la South Sudan

Nthambi yowona za chitetezo ku bungwe la United Nations (UN)lapempha magulu awiri omwe akumenyana mdziko la South Sudan kuti athetse kusamvana komwe kulipo pakati pawo pofuna kupewa zamtopola kuti...

View Article

Kwaya One ya Mtsilo Yapindula ndi Radio Maria Malawi

Kwaya One ya Mtsilo ku parish ya Mponela mu arkidayosizi yaLilongwe ya mpingo wakatolika yati yapindula pa ulendo wake woyendera wailesi ya Maria ku Mangochi. Wapampando wa kwayayi a Rabson Joseph...

View Article

Dayosizi ya Zomba Yapempha Ogwira Ntchito Mchipatala Akhale Olimba pa Chikhristu

Dayosizi ya Zomba ya mpingo wakatolika yapempha akhristu ogwira ntchito muzipatala kuti akhale olimba pa chikhristu chao komanso akuyenera kuzindikira kuti mpingo umawaganizira. Episkopi wa dayosiziyi...

View Article


Mpingo wa Katolika Uyenda Njira ya Mtanda

Mpingo wa katolika mdziko muno komanso mipingo ina ya chikhristu pa dziko lonse lero yachita mwambo wa njira ya mtanda ngati njira imodzi yokumbukira masautso a ambuye yesu khristu. Mwambowu umachitika...

View Article

Boma la Rumphi Likuyembekezeka Kupereka Katemera wa Chikuku kwa Ana 100,000

Ofesi yoona za umoyo m’boma la Rumphi yapempha adindo a m’bomalo kuti awonetsetse kuti ana 95 mwa 1 hundred aliwonse oyambira miyezi 9 mpaka zaka 14 alandire katemera wa matenda a chikuku. Mmodzi mwa...

View Article

Zigawenga 36 za Islamic State Zaphedwa

Zigawenga 36 za gulu la zauchifwamba la Islamic State ISzafa komanso malo omwe zimakhala awonongedwa mdziko la Afghanstan potsatira bomba lomwe linaponyedwa ndi asilikali a mdziko la America. Malinga...

View Article


Bungwe la Worldfish Centre Likufuna Kugwiritsa Ntchito Atolankhani Pomwaza...

Bungwe la Worldfish Centre lati tsopano ligwira ntchito ndi atolankhani pofalitsa uthenga wa zotsatira zakafukufuku yemwe bungweli limachita wokhudza ulimi komanso usodzi wa nsomba. Mkulu wa bungweli...

View Article


Papa Apempha Akhristu Akhale Otumikirana

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti akhale othandizana komanso otumikirana pakati pawo. Papa amalankhula izi ku ndende ina mu mzinda wa Rome pa tsiku...

View Article

Zisankho Zapadera Zichitika Chaka Chino Chisanathe-MEC

Bungwe lowona za chisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lati chisankho chapadera chomwe chalephereka chomwe chimayenera kuchitika m’madera ena a mdziko muno pa 6 June chichitika...

View Article

Papa Akhazikitsa Francisko Komanso Yasinta Kukhala Oyera pa 13 May

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko walengeza kuti akhazikitsa ana awiri omwe anawonekeredwa ndi Amayi Maria ku Fatima, Francisko ndi Yasinta kukhala oyera pa 13 May pa...

View Article

NRB Iyamba Kulembera Ziphaso za Mzika Mwezi wa June

Nthambi yowona za kalembera mdziko muno ya National Registration Bureau (NRB) yati kuyambira mwenzi wa June mpaka December chaka chino liyamba kulemba komanso kupereka ziphaso kwa mzika za dziko lino....

View Article


Bambo Awombera ndi Kupha Wapolisi Mdziko la France

Bambo wina wawombera ndi kupha wa polisi mu mzinda wa Paris mdziko la France. Malipoti a wailesi ya BBC ati mkuluyu anawomberanso apolisi ena awiri omwe avulala kwambiri koma apolisi ena anawomberanso...

View Article

Papa Akuyembekezeka Kuyendera Dziko la Egypt

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko akuyembekezeka kukayendera dziko la Egypt sabata ikudzayi. Malipoti a wayilesi ya Vatican ati mwazina Papa akayendera sukulu ya maphunziro...

View Article


Nduna ya Chitetezo Mdziko la Afganstan Itula Pansi Udindo

Nduna ya za chitetezo ndi mkulu wa asilikali m’dziko la Afghanstan yatula pansi ma udindo wake, kaamba ka kuphedwa kwa asilikali a dzikolo ndi gulu la za uchifwamba la ma Taliban. Malinga ndi malipoti...

View Article

Anthu 24 Afa pa Chiwonetsero Mziko la Venezuella

Anthu akupitilira kufa mdziko la Venezuella pa chiwonetsero chosonyeza kusakondwa ndi utsogoleri wa a Nicholus Maduro chikupitilira ku likulu la dzikolo ku Caracus. Malipoti a wailesi ya BBC ati anthu...

View Article


Papa Achita Nsembe ya Misa ya Maliro a Cardinal Nicora

Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko wachita mwambo wa nsembe ya misa ya maliro a Cardinal Attilio Nicora. Malipoti a wailesi ya Vatican ati mwambowu wachitika lolemba mu...

View Article

Amangidwa Kamba Kopha Munthu ku Machinga

Apolisi m’boma la Machinga akusunga mchitokosi mnyamata wina wa zaka 21 zakubadwa pomuganizila kuti wapha mnyamata wina m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Constable Davie Sulumba wati...

View Article

Mnyamata Afa Atagwidwa ndi Ng’ona

Mnyamata wina wa zaka 14 zakubadwa wafa ng’ona itamugwira pa doko la Kambulire pa nyanja ya Malombe m’boma la Mangochi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Inspector Rodrick Maida watsimikiza za...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>